\v 5 \v 6 Ngati mudzikweza pamwamba panga ndi kundigwiritsa ntchito kunyozeka ndi ine, mudzadziwe kuti Mulungu wandilakwira ndipo wandigwira muukonde wanga.