Fri Oct 01 2021 13:09:13 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-01 13:09:13 +02:00
parent 4efe463b43
commit f6f9b46991
3 changed files with 3 additions and 0 deletions

1
36/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 \v 5 Pakuti mawu anga sadzakhala onama; wina wokhwima mchidziwitso ali nanu. Onani, Mulungu ndi wamphamvu, ndipo sapeputsa aliyense; Ngwamphamvu zopambana zakuzindikira.

1
36/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 \v 7 Sasunga moyo wa anthu oyipa koma m'malo mwake amachita zabwino kwa iwo omwe akuvutika. Samachotsa maso ake kwa olungama koma m'malo mwake amawayika pampando wachifumu ngati mafumu kwamuyaya, ndipo amakwezedwa.

1
36/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 \v 9 Ngati amangidwa maunyolo ndikumangirizidwa mu zingwe zowawa, ndiye amawawululira zomwe adachita, zolakwa zawo ndi kunyada kwawo.