Mon Oct 04 2021 14:40:15 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-04 14:40:16 +02:00
parent 5ecc808129
commit b4f7867c4d
13 changed files with 26 additions and 12 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 8 \v 9 Ngati amangidwa maunyolo ndikumangirizidwa mu zingwe zowawa, ndiye amawawululira zomwe adachita, zolakwa zawo ndi kunyada kwawo.
\v 8 Ngati amangidwa maunyolo ndikumangirizidwa mu zingwe zowawa, \v 9 ndiye amawawululira zomwe adachita, zolakwa zawo ndi kunyada kwawo.

View File

@ -1 +1 @@
\v 10 \v 11 \v 12 Amatseguliranso makutu awo kumachitidwe ake, ndikuwalamula kuti atembenuke kusiya zoipa. Ngati amumvera ndi kum'pembedza, adzakhala masiku awo mosangalala, ndi zaka zawo mokhutira. Komabe, ngati samvera, adzawonongeka ndi lupanga; adzafa chifukwa alibe chidziwitso.
\v 10 Amatseguliranso makutu awo kumachitidwe ake, ndikuwalamula kuti atembenuke kusiya zoipa. \v 11 Ngati amumvera ndi kum'pembedza, adzakhala masiku awo mosangalala, ndi zaka zawo mokhutira. \v 12 Komabe, ngati samvera, adzawonongeka ndi lupanga; adzafa chifukwa alibe chidziwitso.

View File

@ -1 +1 @@
\v 13 \v 14 Anthu osapembedza amasunga mkwiyo wawo; Sapempha thandizo ngakhale Mulungu awamange. Iwo adzafa ali anyamata; miyoyo yawo imathera pakati pa achiwerewere achipembedzo.
\v 13 Anthu osapembedza amasunga mkwiyo wawo; Sapempha thandizo ngakhale Mulungu awamange. \v 14 Iwo adzafa ali anyamata; miyoyo yawo imathera pakati pa achiwerewere achipembedzo.

View File

@ -1 +1 @@
\v 15 \v 16 Mulungu amapulumutsa wozunzika ndi masautso awo; amatsegula makutu awo kupondereza kwawo. Inde, akufuna kukutulutsani m'masautso kupita kumalo opanda mavuto, komanso patebulo panu podzaza ndi mafuta.
\v 15 Mulungu amapulumutsa wozunzika ndi masautso awo; amatsegula makutu awo kupondereza kwawo. \v 16 Inde, akufuna kukutulutsani m'masautso kupita kumalo opanda mavuto, komanso patebulo panu podzaza ndi mafuta.

View File

@ -1 +1 @@
\v 17 \v 18 Koma inu mwadzazidwa ndi chiweruzo kwa anthu oyipa; chiweruzo ndi chilungamo zakugwerani. Musalole mkwiyo wanu kukusokonezeni kuti ukunyozeni, kapena kukula kwa dipo kuti akupatutseni.
\v 17 Koma inu mwadzazidwa ndi chiweruzo kwa anthu oyipa; chiweruzo ndi chilungamo zakugwerani. \v 18 Musalole mkwiyo wanu kukusokonezeni kuti ukunyozeni, kapena kukula kwa dipo kuti akupatutseni.

View File

@ -1 +1 @@
\v 19 \v 20 \v 21 Kodi chuma chanu chingakupindulitseni, kuti musakhale m'mavuto, kapena kodi mphamvu zanu zonse zingakuthandizeni? Musakonde usiku, kuti muchimwire ena, pamene anthu akudulidwa m'malo mwawo. Samalani kuti musatembenukire kuchimo chifukwa mukuyesedwa ndi mavuto kuti mupewe kuchimwa.
\v 19 Kodi chuma chanu chingakupindulitseni, kuti musakhale m'mavuto, kapena kodi mphamvu zanu zonse zingakuthandizeni? \v 20 Musakonde usiku, kuti muchimwire ena, pamene anthu akudulidwa m'malo mwawo. \v 21 Samalani kuti musatembenukire kuchimo chifukwa mukuyesedwa ndi mavuto kuti mupewe kuchimwa.

View File

@ -1 +1 @@
\v 22 \v 23 \v 24 Taonani, Mulungu ali wokwezeka ndi mphamvu yake; ndani mphunzitsi ngati iye? Ndani adamulangiza za njira yake? Ndani angamuuze kuti, 'Wachita zosalungama?' Kumbukirani kuyamika ntchito zake, zomwe anthu adayimba.
\v 22 Taonani, Mulungu ali wokwezeka ndi mphamvu yake; ndani mphunzitsi ngati iye? \v 23 Ndani adamulangiza za njira yake? Ndani angamuuze kuti, 'Wachita zosalungama?' \v 24 Kumbukirani kuyamika ntchito zake, zomwe anthu adayimba.

View File

@ -1 +1 @@
\v 25 \v 26 Anthu onse adaziwona izi, koma amangowona kutali. Onani, Mulungu ndi wamkulu, koma ife sitikumumvetsa iye; Zaka zake ndi zambiri.
\v 25 Anthu onse adaziwona izi, koma amangowona kutali. \v 26 Onani, Mulungu ndi wamkulu, koma ife sitikumumvetsa iye; Zaka zake ndi zambiri.

View File

@ -1 +1 @@
\v 27 \v 28 \v 29 Pakuti iye amakoka madontho a madzi amene amawasandutsa mvula kuchokera ku nthunzi yake, imene mitambo imagwetsa ndi kutsanulira zochuluka pa anthu. Zowonadi, kodi pali amene angamvetsetse kufalikira kwa mitambo ndi bingu kuchokera kuchinyumba chake?
\v 27 Pakuti iye amakoka madontho a madzi amene amawasandutsa mvula kuchokera ku nthunzi yake, \v 28 imene mitambo imagwetsa ndi kutsanulira zochuluka pa anthu. \v 29 Zowonadi, kodi pali amene angamvetsetse kufalikira kwa mitambo ndi bingu kuchokera kuchinyumba chake?

View File

@ -1 +1 @@
\v 30 \v 31 Taonani, ayala ndi mphezi pakamwa pake, Naphimba mizu ya nyanja. Potero amaweruza anthu, napereka chakudya chochuluka.
\v 30 Taonani, ayala ndi mphezi pakamwa pake, Naphimba mizu ya nyanja. \v 31 Potero amaweruza anthu, napereka chakudya chochuluka.

View File

@ -1 +1 @@
\v 32 \v 33 Amadzaza manja ake ndi mphezi mpaka atawalamula kuti amenye. Bingu lake limachenjeza za mkuntho, ng'ombe zimamvanso kuti zikubwera.
\v 32 Amadzaza manja ake ndi mphezi mpaka atawalamula kuti amenye. \v 33 Bingu lake limachenjeza za mkuntho, ng'ombe zimamvanso kuti zikubwera.

1
37/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 37

View File

@ -427,6 +427,19 @@
"35-15",
"36-title",
"36-01",
"36-04"
"36-04",
"36-06",
"36-08",
"36-10",
"36-13",
"36-15",
"36-17",
"36-19",
"36-22",
"36-25",
"36-27",
"36-30",
"36-32",
"37-title"
]
}