Sun Oct 03 2021 16:49:14 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 16:49:15 +02:00
parent 335ba07cfe
commit 592a23cc33
5 changed files with 8 additions and 3 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 23 \v 24 \v 25 Kodi zolakwa zanga ndi machimo anga zingati? Ndidziwitseni kulakwa kwanga ndi tchimo langa. Bwanji mukundibisira nkhope yanu ndipo mukunditenga ngati mdani wanu? Kodi muzunza tsamba lothamangitsidwa? Kodi mukuthamangitsa mapesi ouma?
\v 23 Kodi zolakwa zanga ndi machimo anga zingati? Ndidziwitseni kulakwa kwanga ndi tchimo langa. \v 24 Bwanji mukundibisira nkhope yanu ndipo mukunditenga ngati mdani wanu? \v 25 Kodi muzunza tsamba lothamangitsidwa? Kodi mukuthamangitsa mapesi ouma?

View File

@ -1 +1 @@
\v 26 \v 27 \v 28 Popeza umandilembera zinthu zowawa; Mwandipatsa cholowa cha zoyipa za unyamata wanga. Munakhazikitsanso mapazi anga m'matangadza; mumayang'anitsitsa njira zanga zonse; mumasanthula malo omwe mapazi anga amayenda ngakhale ndili ngati chovunda chomwe chatha, ngati chovala chomwe njenjete zadya.
\v 26 Popeza umandilembera zinthu zowawa; Mwandipatsa cholowa cha zoyipa za unyamata wanga. \v 27 Munakhazikitsanso mapazi anga m'matangadza; mumayang'anitsitsa njira zanga zonse; mumasanthula malo omwe mapazi anga amayenda \v 28 ngakhale ndili ngati chovunda chomwe chatha, ngati chovala chomwe njenjete zadya.

View File

@ -1 +1 @@
\c 14 \v 1 \v 2 \v 3 Munthu wobadwa ndi mkazi amakhala m'masiku ochepa, nakhuta mavuto. Amamera m'nthaka ngati duwa, ndipo wadulidwa; athawa ngati mthunzi, osakhalitsa. Kodi mumayang'ana chilichonse cha izi? Kodi ukundiweruza?
\c 14 \v 1 Munthu wobadwa ndi mkazi amakhala m'masiku ochepa, nakhuta mavuto. \v 2 Amamera m'nthaka ngati duwa, ndipo wadulidwa; athawa ngati mthunzi, osakhalitsa. \v 3 Kodi mumayang'ana chilichonse cha izi? Kodi ukundiweruza?

1
14/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 14

View File

@ -174,6 +174,10 @@
"13-13",
"13-16",
"13-18",
"13-20",
"13-23",
"13-26",
"14-title",
"14-07",
"14-10",
"14-13",