Sun Oct 03 2021 17:22:45 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 17:22:45 +02:00
parent 609d39b576
commit 495aa60af2
7 changed files with 13 additions and 6 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 31 \v 33 Tcherani khutu, Yobu, ndi kundimvera; khalani chete ndipo ndiyankhula. \v 32 Ngati muli ndi chilichonse choti mundiyankhe, ndiyankheni; lankhula, chifukwa ndikufuna ndikutsimikizire kuti ukunena zowona. Ngati sichoncho, ndimvereni; khalani chete, ndipo ndikuphunzitsani nzeru. "
\v 31 Tcherani khutu, Yobu, ndi kundimvera; khalani chete ndipo ndiyankhula. \v 32 Ngati muli ndi chilichonse choti mundiyankhe, ndiyankheni; lankhula, chifukwa ndikufuna ndikutsimikizire kuti ukunena zowona. \v 33 Ngati sichoncho, ndimvereni; khalani chete, ndipo ndikuphunzitsani nzeru. "

View File

@ -1 +1 @@
\c 34 \v 1 \v 2 \v 3 Elihu anapitiriza kulankhula kuti: “Tamverani mawu anga, anzeru inu, ndimvereni, inu akudziwa. Pakuti khutu liyesa mawu, monga m'kamwa mulawa kulawa.
\c 34 \v 1 Elihu anapitiriza kulankhula kuti: \v 2 “Tamverani mawu anga, anzeru inu, ndimvereni, inu akudziwa. \v 3 Pakuti khutu liyesa mawu, monga m'kamwa mulawa kulawa.

View File

@ -1 +1 @@
\v 4 \v 5 \v 6 Tiyeni tisankhe tokha chomwe chiri cholungama: tizindikire pakati pathu chomwe chili chabwino. Pakuti Yobu anati, 'Ine ndine wolungama, koma Mulungu wandilanda. Kaya ndili ndi ufulu wotani, ndimaonedwa kuti ndine wabodza. Chilonda changa sichitha, ngakhale ndilibe uchimo. '
\v 4 Tiyeni tisankhe tokha chomwe chiri cholungama: tizindikire pakati pathu chomwe chili chabwino. \v 5 Pakuti Yobu anati, 'Ine ndine wolungama, koma Mulungu wandilanda. \v 6 Kaya ndili ndi ufulu wotani, ndimaonedwa kuti ndine wabodza. Chilonda changa sichitha, ngakhale ndilibe uchimo. '

View File

@ -1 +1 @@
\v 7 \v 8 \v 9 Ndi munthu uti amene angafanane ndi Yobu, amene amamwa zopanda pake ngati madzi, amene amayenda m thegulu la anthu ochita zoyipa, ndipo amayenda ndi anthu oyipa? Pakuti iye anati, 'Sizothandiza kwa munthu kusangalala ndi zinthu zimene Mulungu amafuna.'
\v 7 Ndi munthu uti amene angafanane ndi Yobu, amene amamwa zopanda pake ngati madzi, \v 8 amene amayenda m thegulu la anthu ochita zoyipa, ndipo amayenda ndi anthu oyipa? \v 9 Pakuti iye anati, 'Sizothandiza kwa munthu kusangalala ndi zinthu zimene Mulungu amafuna.'

View File

@ -1 +1 @@
\v 10 \v 11 \v 12 Chifukwa chake, ndimvereni, inu anzeru: kuti kutari ndi Mulungu kuchita zoyipa; kukhale kutali ndi Wamphamvuyonse kuchita tchimo. Pakuti amabwezera ntchito ya munthu; amachititsa munthu aliyense kubwezera mphotho ya njira zake. Ndithudi, Mulungu sachita choipa chilichonse, ndipo Wamphamvuyonse sapotoza chiweruzo.
\v 10 Chifukwa chake, ndimvereni, inu anzeru: kuti kutari ndi Mulungu kuchita zoyipa; kukhale kutali ndi Wamphamvuyonse kuchita tchimo. \v 11 Pakuti amabwezera ntchito ya munthu; amachititsa munthu aliyense kubwezera mphotho ya njira zake. \v 12 Ndithudi, Mulungu sachita choipa chilichonse, ndipo Wamphamvuyonse sapotoza chiweruzo.

1
34/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 34

View File

@ -401,6 +401,12 @@
"33-23",
"33-25",
"33-27",
"33-29"
"33-29",
"33-31",
"34-title",
"34-01",
"34-04",
"34-07",
"34-10"
]
}