Sun Oct 03 2021 16:45:09 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 16:45:09 +02:00
parent 71203be2b8
commit 30febdc43f
6 changed files with 11 additions and 4 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 24 \v 25 Amachotsa kumvetsetsa kwa atsogoleri a anthu padziko lapansi; awachititsa kuti ayendeyende m'chipululu momwe mulibe njira. Afufuza mumdima wopanda kuunika; amawachititsa kudzandama ngati munthu woledzera.
\v 24 Amachotsa kumvetsetsa kwa atsogoleri a anthu padziko lapansi; awachititsa kuti ayendeyende m'chipululu momwe mulibe njira. \v 25 Afufuza mumdima wopanda kuunika; amawachititsa kudzandama ngati munthu woledzera.

View File

@ -1 +1 @@
\c 13 \v 1 \v 2 Taonani, diso langa laona izi zonse; khutu langa lamva, nazimvetsa. Zomwe mukudziwa, inenso ndikudziwa; Sindine wotsika kwa inu.
\c 13 \v 1 Taonani, diso langa laona izi zonse; khutu langa lamva, nazimvetsa. \v 2 Zomwe mukudziwa, inenso ndikudziwa; Sindine wotsika kwa inu.

View File

@ -1 +1 @@
\v 3 \v 4 \v 5 Komabe, ndingakonde kulankhula ndi Wamphamvuyonse; Ndikufuna kukambirana ndi Mulungu. Koma inu mukuyeretsa choonadi ndi mabodza; inu nonse ndinu asing'anga opanda pake. Mwenzi mutakhala chete! Ikanakhala nzeru yako.
\v 3 Komabe, ndingakonde kulankhula ndi Wamphamvuyonse; Ndikufuna kukambirana ndi Mulungu. \v 4 Koma inu mukuyeretsa choonadi ndi mabodza; inu nonse ndinu asing'anga opanda pake. \v 5 Mwenzi mutakhala chete! Ikanakhala nzeru yako.

View File

@ -1 +1 @@
\v 6 \v 7 \v 8 Tamverani tsopano malingaliro anga; mverani kuchonderera kwa milomo yanga. Kodi mudzalankhulira Mulungu zosalungama, ndi kundinenera zachinyengo? Kodi mumuwonetsa tsankho? Kodi mufuna kutsutsana ndi Mulungu?
\v 6 Tamverani tsopano malingaliro anga; mverani kuchonderera kwa milomo yanga. \v 7 Kodi mudzalankhulira Mulungu zosalungama, ndi kundinenera zachinyengo? \v 8 Kodi mumuwonetsa tsankho? Kodi mufuna kutsutsana ndi Mulungu?

1
13/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 13

View File

@ -163,6 +163,12 @@
"12-13",
"12-16",
"12-19",
"12-22",
"12-24",
"13-title",
"13-01",
"13-03",
"13-06",
"14-07",
"14-10",
"14-13",