Sun Oct 03 2021 16:12:03 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-03 16:12:04 +02:00
parent 608a85f4b0
commit 219459d30d
7 changed files with 12 additions and 5 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 27 \v 28 Izi ndi zowona, ngakhale adabisa nkhope yake ndi mafuta ake, nadzola mafuta m'chuuno mwake, nakhala m'midzi yopasuka; m'nyumba zomwe palibe munthu amene akukhalamo panopo ndipo zatsala pang'ono kuunjika milu.
\v 27 Izi ndi zowona, ngakhale adabisa nkhope yake ndi mafuta ake, nadzola mafuta m'chuuno mwake, \v 28 nakhala m'midzi yopasuka; m'nyumba zomwe palibe munthu amene akukhalamo panopo ndipo zatsala pang'ono kuunjika milu.

View File

@ -1 +1 @@
\v 29 \v 30 Sadzakhala wachuma; Chuma chake sichidzakhalitsa ndipo chuma chake sichidzafalikira padziko lapansi. Sadzatuluka mumdima; lawi lidzaumitsa mapesi ake; adzachoka pakamwa pa Mulungu.
\v 29 Sadzakhala wachuma; Chuma chake sichidzakhalitsa ndipo chuma chake sichidzafalikira padziko lapansi. \v 30 Sadzatuluka mumdima; lawi lidzaumitsa mapesi ake; adzachoka pakamwa pa Mulungu.

View File

@ -1 +1 @@
\v 31 \v 32 \v 33 Asamadalire zopanda pake, kudzinyenga yekha; pakuti zopanda pake zidzakhala mphotho zake. Zidzachitika nthawi zake zisanafike; nthambi yake sidzakhala yobiriwira. Adzaponya mphesa zake zosapsa ngati mpesa; adzataya maluwa ake ngati mtengo wazitona.
\v 31 Asamadalire zopanda pake, kudzinyenga yekha; pakuti zopanda pake zidzakhala mphotho zake. \v 32 Zidzachitika nthawi zake zisanafike; nthambi yake sidzakhala yobiriwira. \v 33 Adzaponya mphesa zake zosapsa ngati mpesa; adzataya maluwa ake ngati mtengo wazitona.

View File

@ -1 +1 @@
\v 34 \v 35 Pakuti gulu la osapembedza lidzakhala lopanda kanthu; moto udzawononga mahema awo a ziphuphu. Amakhala ndi pakati pa choyipa, nabala mphulupulu; mimba yawo imakhala ndi chinyengo. "
\v 34 Pakuti gulu la osapembedza lidzakhala lopanda kanthu; moto udzawononga mahema awo a ziphuphu. \v 35 Amakhala ndi pakati pa choyipa, nabala mphulupulu; mimba yawo imakhala ndi chinyengo. "

View File

@ -1 +1 @@
\c 16 \v 1 \v 2 \v 3 Pamenepo Yobu anayankha nati, "Ndamva zinthu zambiri zotere; nonsenu ndinu otonthoza omvetsa chisoni. Kodi mawu opanda pake adzatha? Kodi muli ndi vuto lanji kuti muyankhe chonchi?
\c 16 \v 1 \v 3 Pamenepo Yobu anayankha nati, \v 2 "Ndamva zinthu zambiri zotere; nonsenu ndinu otonthoza omvetsa chisoni. Kodi mawu opanda pake adzatha? Kodi muli ndi vuto lanji kuti muyankhe chonchi?

1
16/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 16

View File

@ -161,6 +161,12 @@
"15-17",
"15-19",
"15-22",
"15-25",
"15-27",
"15-29",
"15-31",
"15-34",
"16-title",
"19-title",
"21-title",
"21-01",