Wed May 26 2021 19:00:17 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2021-05-26 19:00:20 +02:00
commit 7ac037488c
386 changed files with 823 additions and 3 deletions

1
01/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 1 \v 1 Pachiyambi panali mau ,ndipo mau anali ndi Mulungu,ndipo mau anali Mulungu. \v 2 uyu anali pachiyambi ndi Mulungu. \v 3 Zonse zinalengedwa na iye ndipo palibe chamene chinalengedwa popanda iye.

1
01/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Mwayeve mwenze umoyo na umoyo wenzeli kuunika kwabanthu onse . \v 5 kuunika kunaonekela mumdima koma mudima siunakwanise kuigonjesa.

1
01/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Penze munthu wamene anachokela kwa Mulungu amene anali Yohane \v 7 Anabwela kupelekela umboni nyali kuti anthu onse akakhulupilile kupitila mulieve. , \v 8 Yohane sanali Nyali koma anabwela kupeleka umboni kuti nyali.

1
01/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Inali nyali yazoona isanika ku anthu onse lapansi,yamene inabwela mu ziko lapansi.

1
01/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Eve enze muziko lapansi na vonse \v 11 Niyeve anavipanga koma sibanamuzibe,anabwela kubanthu bake koma sibanamulandile nafuti sibanamukhulukile

1
01/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 koma kuli onse anamulandila,anamukhulupilila anabapasa mupata kunkhala bana ba Mulungu. \v 13 osati bana obadwa na mwazi kapena kubadwa muchifunilo cha munth, koma obadwa mwachifunilo cha Mulungu.

1
01/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Mau anasanduka munthu nabwela kunkhala pakati ise ,tinaona ulemelelo wochekela kwa iye yeka ochokela kwa Atate,wozula na chisomo na choonadi. \v 15 Yohane anachitila umboni paliyeve ,nakupunda kuti"Uyu niwamene ninakambapo,iye obwela pasogolo,apambana ine pakuti analiko.

1
01/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 koma kuchokela kwayeve kuchokela chisomo pamwamba pa chisomo, \v 17 lamulo inabwela na Mose koma cisoma na choonadi vinabwela na yesu Christu. \v 18 kulibe wamene anaona mulungu panthawi iliyonse,.Mulungu yeve eka wamene apumulila pachifuwa cha Atate,Amene apumulila pa chifuba cha Atate ndiye avumbulusa Atate.

1
01/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 Uyu ndiye umboni wa Yohane pamene Ayuda atuma Ansembe na Alevy kuchokela ku Yerusalem kumufunsa kuti "Nanga ndiwe ndani ?Ndiwe Eliya,ndiwe Muneneri kapena ndiwe mesiya? \v 20 Yohane anabauza vazoona kuti ine sindine Christu, \v 21 Anamunsa nisnhi ndiwe ndani?Eliya?Anakamba kuti sindine,Nanga ndiwe muneneri?anati sindine

1
01/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 Banamufunsa Yohane kuti tiuze ndiwe ndani kuti tipeleke yankho kuli bamene batituma,"ukamba chani pali wemwine? \v 23 Anabayankha kuti ine ndine chabe mau yofuula mu chipululu kuti " konzani njira yambuye siteleti,monga momwe muneneri yesaya ananenera.

1
01/24.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 24 Baja bamene banatumiwa anatumiwa na Afarisi \v 25 Amufunsa kuti "Nanga nichifukwa ninji ubatiza banthu pamene wakana kuti sindiwe Eliya,Muneneri kapena Christu?

1
01/26.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 26 Yohane anabayankha kuti Ine nibatiza na manzi,koma alipo pakati kanu wamene simuziwa,wamene nansapato zake sinikwanisa kumasula, \v 27 Abwela pasogolo panga. \v 28 zonsezi zinachitika ku Berthany kuja kumbali kwa Yolodani,kwamene Yohane anali kubatiza.

1
01/29.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 29 Kuseni kwakaena Yohane anaona Yesu alikubwela kwa eve nokamba ati""Taonani Nkhosa yochokela kwa Mulungu amene achosa machimo laziko lapansi. \v 30 Uyu niwamene ninakambapo kuti kuli wamene azabwela wamene,iye wamene abwela pambuyo panga "nimukulu kuchila ine chifukwa analiko, \v 31 sininamuzibe koma chinkhala tele kuti akavumbulusidwe kwa Israeli kuti ninabwela kubatiza na manzi..

1
01/32.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 32 Ndipo Yohane anachitila umboni kuti ninaona muzimu Oyera alikubwela pa iye monga nkhunda kuchokela kumwamba,muzimu unakhala pa eve. \v 33 sininamuzindikile iye koma amene ananituma kubatiza na manzi ananaiuza kuti amene Muzimu uzasikila,nakukhala paiye. ndiye wamene abatiza ndi Muzimu Oyera. \v 34 nayangana nakuchitila umboni kuti nimwana wa Mulungu.

1
01/35.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 35 Kuseni kokonkhapo Yohane anali naophunzila bake babili \v 36 ,Anaona Yesu alikuyenda nati" Taonani Nkhosa ya Mulungu"

1
01/37.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 37 Ndipo ophunzila ace anamumvela alikulankhula izi \v 38 Ndipo anamulondola iye.ndipo yesu anabafunsa kuti "mufuna chani ,anati muphunzisi kubondi nikuti? \v 39 Anati Tiyeni mukaone anapita naye yesu kunyumba kwake chifukwa inalinso nthawi yamumazulo.

1
01/40.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 40 Umozi waiwo amene anamvela Yohane kulankhula nalondola Yesu anali Andeleya mubale wa simon Petro, \v 41 Anapeza mubale wake Petro poyamba namuuza nati"Tamupeze Mesiya(kutanthauza Christu) \v 42 Atamubwelesa kwa Yesu anaona iye ,Anati "Ndiwe Simon mwana wa Yohane koma kuyambila lelo uzachedwa Cephas(kutanthauza Petro)

1
01/43.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 43 Siku yokonkhapo pamene Yesu anafuna kupita ku Galileya akumana ndi Philip ndipo anamuuza kuti amulondole. \v 44 Manje Philip anali kuchokela ku Betsaida komwe Andeleya ndi Petro anali kuchokela. \v 45 Pamene philipe anapeza Natan anamuuza nati Tamupeza uja wamene Mose anakambapo mumalamulo na aneneri kale paja ,mwana wa Yosefe waku Nazareti.

1
01/46.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 46 Natan anafunsa Philip kuti "Nichani Chabwino chingachoke ku Nazareti?Ndipo anati tiye uwone, \v 47 Pamene Yesu anamuona anati "Taonani Israeli weni weni amene mwaiye mulibe chinyengo. \v 48 Natan anafunsa kodi waniziba bwani?Yesu anamuuza kuti pamene mukalibe kuwonana na Philip Nenze nakuona ninshi ulinkhale panyansi pa chimtengo cha Mkuyu.

1
01/49.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 49 Ndipo Natan anamuyankha kuti Muphunzisi ndinu mwana wa Mulungu, \v 50 Ndimwe mfumu ya israeli. Yesu anamuuza kuti , chifukwa chakuti nakuona panyansi wa mtengo waMkuyu ndiye pamene ukhulupilila? Yesu anamuuza kuti uzaona vikulu kupambana ivi. \v 51 Nikamba chazooona kwaiwe uzaona kumwamba kuzaseguka nangelo ba Mulungu nakwela nakuseluka pali mwana wamunthu.

1
01/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 1

1
02/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 2 \v 1 Panapita masiku yatatu pamene kunankhala ukwati ku kana wa ku Galileya, na amai bake ba Yesu analiko ku ukwati uyu. \v 2 Yesu ndi opunzila bake anaitanidwa ku pezekako ku ukwati.

1
02/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Kunapezeka kuti vinyu inasila, amai bake Yesu ana muuza kuti, ''vinyu yasila.'' \v 4 Yesu anakamba kuti, ''muzimai, nichani ubwela kuline? popeza kuti ntawi yanga ikalibe kufika.'' \v 5 Amai bake ba Yesu banauza banchito kuti, ''chilichonse chamene akamba kuli iwe, chitani.''

2
02/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1,2 @@
\v 6 Panapezeka kuti,kunali nongo zili 6 zamene zinali kusebenza mumwambo wosambilamo waba yuda , iliyonse inali na muyeso wa 80 na 120 litazi. \v 7 Yesu anabauza kuti,
''azuzye aya manongo na manzi'' . Ndipo banazulisa maningi. \v 8 Ndipo anauziwa banchito, ''kutengamo manzi ena na kupasa mukulu ogabanisa.'' Ndipo anachita.

1
02/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Uyu mukulu ogabanisa manzi pamene analabamo mu manzi,anapeza kuti ni vinyu, chinamudabwisa koma, (banchito bamene banatapa yaja manzi banali kuziba ). Anaitana mukwatibwi ndipo anamuuza kuti, \v 10 Uyu mukulu ogabisa anapita ku mukwatibwi nakumuuza kuti, '' Muntu aliyense apasa vinyu vabwino pachiyambi ndipo zo chipa kumasilizilo kuchila manje.''

1
02/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Ichi chinali chodabwisa choyamba chamene Yesu anachita mumuzinda wa kana wa mu Galileya. Anavumbulusa ulemelelo wake ndipo wopunzila bake banakulupilila.

1
02/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Kuchoka apo Yesu, bamai bake, babale bake, na wopunzila bake banapita ku kapenamu na kunkalako masiku yango'no.

1
02/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Manje ntawi ya paskha yaba yuda inali pafupi, ndipo Yesu anayenda ku yelusalema. \v 14 Yesu anapeza ogulisa ng'ombe, mbelele, na nkunda nawochinjanisa ndalama balinkale.

1
02/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 Ndipo anapanga mukwapu nakuchosamo bonse mukachisi, kufakilako mbelele na ngo'mbe. Anachosa baja bamalonda wochinja ndalama na kupindimula ma tebulo yao. \v 16 Kuli baja wogulisa nkhunda anabauza kuti, ''chosani ivi vonse, Siyani kusandusa nyumba yaba tate kunkala yogulisilamo.''

1
02/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 WopunzhiLa bake Banakumbuka kuti nicholembenwa , '' kuti chilakolako cha nyumbayanu chanidya''. \v 18 Pamene apo bayuda bana mufunsa kuti, '' kodi ni chiziwiso chabwanji chamene muzatilangiza, chifukwa muchitilamo zonse izi''. \v 19 Na Yesu anabauza kuti, ''Pwanyani kachisi iyi, ine nizamanga masiku yatatu.''

1
02/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 Koma, bakulu ba yuda banakamba kuti kodi, ungamange bwanji kachisi iyi mumasiku yatatu popeza kuti tinamanga mu zaka zili 46"? \v 21 Koma , Yesu anali kukamba pakachisi yatupiyake. \v 22 Pamene anauka kubakufa,ophunzila bake banakumbukila chamene Yesu anakamba mumalemba mumakambidwe yake na kukulupilila malemba yamene anakamba.

1
02/23.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 23 Koma pamene anali phwando ya pasakha muyelusalemu, bambili bamene banabwela bana kulupilila muzina yake pamene banaona zichitidwe zake. \v 24 Koma, Yesu sianakulupilile ali onse chifukwa analikuziba zinali mumutima mwao, \v 25 chifukwa sianalikufunikila wina kupasila umboni pa munthu chifukwa analikuziba zonse zamukati mwamunthu.

1
02/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
MUTU 2

1
03/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 3 \v 1 Koma kunali mu farisi oyitanidwa Nikodema, musogoleli wa Ayuda. \v 2 Uyu muntu anabwela kuli Yesu usiku na kufunsa, " Apunzisi, tiziba kuti ndimwe apunzisi ochokela kwa Mulungu chifukwa kulibe wamene angachite zodabwisa ngati sachokela kwa Mulungu.

1
03/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Yesu ana yanka ati, "chonadi, chonadi, ngati muntu sanabadwe mwasopano, sangaone ufumu wa Mulungu." \v 4 Nikodema ana kamba kuli iye, " Kodi munthu angabadwe kachibiri ngati ni mukulu ?" Sangabadwe kabiri mumimba yaba maibake, kodi chingachitike?"

1
03/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Yesu ana yanka," chonadi, chonadi,ngati muntu sanabadwe ku manzi na ku mu Zimu, sangalowe mu ufumu wa Mulungu. \v 6 Obadwa ku tupi ni tupi, obadwa ku mu Zimu ni muzimu.

1
03/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Usadabwe kuti na lankula kuri iwe, ' ufunika kubadwa mwasopano.' \v 8 Mpepo imachayika konse kwamene ifuna; umavela chongo, koma suziba kwe ichokela na kwamene iyenda. Niponso, ndiye onse amene anabadwa mwa mu Zimu.'

1
03/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Nikodema ana yanka kwa iye ati, "zingateke bwanji izi?" \v 10 Yesu anayanka kwa iye, "kodi ndiwe mupunzisi wa Isirayeli, ndiponso sunvesesa izi zinthu? \v 11 Chonadi, chonadi, ni kuuza iwe, ti lankula vetiziba, ndiponso tilina umboni pali vamene tinaona. Koma suvomela umboni watu.

1
03/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Ngati na kuwuza pa zintu za pa ziko ndiponso sunakulupirile, uzakulupirila bwanji zintu za kumwamba? \v 13 Kuribe ana pita ku Mwamba koma iye wamene ana bwela kuchokela ku Mwamba: Mwana wa Muntu.

1
03/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Monga Mose ana kwezeka njoka m'chipululu, chimozimozi Mwana wa Muntu ayenera kukwezedwa, \v 15 kuti onse akulupirila mwa iye azankhala na umoyo osata.

1
03/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Pakuti Mulungu anakonda ziko lapansi, ndiponso anapasa mwana wake iye yekha kuti onse wakulupirila iye asatayike koma ankale na umoyo osata. \v 17 Pakuti Mulungu sanatume mwana wake paziko lapansi kuti akaweruze ziko lapansi koma kuti likapulumusidwe ndi iye. \v 18 Onse amene akulupirila mwa iye sazakaweruzidwa, koma amene sakulupirila iye azaweruzidwa chifukwa sana kulupirile mu zina ya Mwana wa Mulungu yekha.

1
03/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 Koma ciweruziro ndi ici: kuti nyali ya bwela pa ziko lapansi, ndiponso anthu ana kondesesa mu dima kuchila nyali cifukwa machitidwe yao yanali yoipa. \v 20 Pakuti onse amene akonda zoipa azonda nyali elo sanga bwele ku nyali chifukwa machitidwe yake yanga onekele. \v 21 Koma ochita chonadi abwela ku nyali kuti nchito zake, zionekere kuti zinachitidwa mwa Mulungu."

1
03/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 Ku choka apo, Yesu ndiwo punzila bake anapita kuziko la Yudeya. Kuja ana nkala na apunzisi ake na kubatiza bantu bambiri. \v 23 Manje Yohane anali kubatiza mu Ainoni pafupi na Salimu chifukwa kunali manzi yambiri. Bantu banari kubwela kwa iye ndiponso anabatiziwa, \v 24 pakuti Yohane anali akalibe kutayiwa mu jere.

1
03/25.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 25 Pameneapo panauka kushushana pakati ka ena apunzisi aYohane ndi umozi wa aYuda kamba ka mwambo osambikana. \v 26 Ba nayenda kuli Yohane nakukamba kuli iye, " Apunzisi, uja wamene mwenze naye kumbali ya musinje wa Chimana cha Yodani, apasila umboni, onani, ali kubatiza, elo bonse bamukonka iye."

1
03/27.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 27 Yohane ana yanka ati, " Munthu sangalandile koma chapasidwa kuchokela ku mwamba. \v 28 Imwe mweka mungapase umboni kuti anakamba, ' Ine sindine Christu' koma, ' Nina tumiwa pamene akalibe kubwela.'

1
03/29.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 29 Mukwati nimukazi wa kwatibwi. Manje munzake wa mukwatibwi, wamene amaimilila nakumvela, amasangalala maningi chifukwa cha liwu lamukwatibwi. Nimuli ichi, mwamene chisangalalo changa chisilizika. \v 30 Iye afunika kukula, koma ine nichepe.

1
03/31.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 31 Iye wochokela Kumwamba ni wopambana kuchila zonse. Iye ana chokela paziko ni wapaziko ndiponso alankhula zapaziko. Iye wamene achokela Kumwamba achila zonse. \v 32 Amapasa umboni pazamene awona nakumvela, koma kulibe avomeleza umboni wa iye. \v 33 Iye amene ana landila umboni avomekeza kuti Mulungu ndi chonadi.

1
03/34.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 34 Iye wamene Mulungu ana tuma amakamba pa mawu ya Mulungu. Samapasa muzimu ndi muyeso. \v 35 Atate anakonda Mwana ndiponso anapasa zinthu zonse mumanja yake. \v 36 Iye amene akhulupilira mu Mwana azankala na umoyo wosata. Koma amene savelela Mwana sazakaona umoyo, koma ukali wa Mulungu uzankala pali iye.

1
03/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 3

1
04/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 4 \v 1 Manje pamene Yesu anaziba kuti Bafalisi bananvela kuti Yesu anali kupanga na batiza bopunzila ba mbili kuchila Yohane \v 2 (chingankale siYesu wamene anali kubatiza koma bopunzila bake ndiye banali kubatiza), \v 3 Anachokamo mu Yudeya nakubwerela ku Galileya.

1
04/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Koma chenzofunika kuti apitiletu mu Samariya. \v 5 Iye anangena mu komboni ya mu Samariya yamene inali kuitaniwa Sukari, iyi komboni, yenze pafupi na malo yamene Yakobo anapasa mwana wake wa chimuna Yosefe.

1
04/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Chisime cha Yakobo chenzepo. Yesu anafuna kupumulako chifukwa ulendo unamulemesa. Ntawi yenze kuma 12. \v 7 Muzimayi waku Samariya anabwela kutapa manzi pamena paja pa chisime, Yesu anamuuza ati, "iwe muzimayi nipaseko manzi nimwe." \v 8 Ndipo bopunzila bake sibenzepo chifukwa banabwelela mu komboni mukugulako vakudwa.

1
04/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Manje muzimayi waku Samariya anayanka Yesu ati, "nanga nichani iwe wachi Yuda upempha manzi kwaine muzimayi wachi Samariya?" Chifukwa bantu ba Yudeya na bantu ba Samariya sibayendelana. \v 10 Yesu naye anamuyanka kuti, "sembe wenzekuziba mphaso ya Mulungu, na wamene akuuza ati 'nipase chakumwa,' sembe wamupempha, nayeve sembe akupasako manzi ya moyo wosasila."

1
04/11.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 11 Muzimayi anakamba kuti, "Bambo, baketi yotapilako manzi mulibe, ichi chisime nichitali. Nanga manzi ya moyo muzayachosa kuti? \v 12 Sindiwe mukulu, mungamuchile tate wathu Yakobo, anatipasa chisime chamene ichi, nakumwamo eve pamozi nabana bake bamuna na vobeta vake?"

1
04/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Yesu anayanka muzimayi ati, "wonse akumwa manzi yamene yachoka pa chisime ichi azanvela futi njota, \v 14 koma uyo wamene akumwa manzi yamene ine nipasa sazanvela njota futi. Ndipo manzi yamene nizamupasa yanzankala kasupe ka manzi mwayeve yo leta umoyo osasila."

1
04/15.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 15 Muzimayi anamuuza kuti, "Bambo, nipaseni manzi yamene ayo nimweko pakuti, nisankanvele njota futi nileke kubwelanso kuno ku chisime mukatapa manzi masiko onse." \v 16 Yesu naye anamuyanka kuti, "iwe yenda ku nyumba kwako uyitane mwamuna wako, mubwele bonse kuno."

1
04/17.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 17 Muzimayi anamuyanka kuti, "nilibe mwamuna." Yesu anayanka kuti, "ndipo wakamba zoona kuti ulibe mwamuna, \v 18 chifukwa iwe unakwatiwapo ku ba muna bali 5, ndipo wamene uli naye apa simwamuna wako. Chamene wakamba ni chazoona."

1
04/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 Muzimayi anakamba kuti, "Bambo, naona kuti imwe ndimwe muneneli. \v 20 Makolo batu banalambila pa luphiri apa, koma imwe mukamba ati ku Yerusalemu ndiye kumalo kwamene bantu bafunika kulambilila."

1
04/21.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 21 Yesu anamuuza kuti, "nikulupilile ine, muzimayi, ntawi ibwela yamene simuzalambila Tate pa phili apa, kapena mu Yerusalemu. \v 22 Imwe mulambila chamena simuziba. Ife tilambila chamene tiziba, chifukwa chipulumuso chichokela kwa Ayuda.

1
04/23.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 23 Koma, ntawi ibwela ndipo ntawi yafika, yamene bolambila ba zoona bazalambila batate mu muzimu na mu choonadi; chifukwa Batate basakila banthu basochabe kuti bankale womulambila. \v 24 Mulungu ni Muzimu, ndipo bonse bolambila bafunika kulambila Ambuye mu muzimu na muchoonadi.

1
04/25.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 25 Muzimayi anakamba kuli eve kuti "niziba kuti Mesiya abwela, (wamene aitaniwa Kristu). Akabwela azatipunzisa zintu zonse." \v 26 Yesu anamuuza kuti, "ndine wamene, wamene akamba naiwe."

1
04/27.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 27 Pa ntawi yamene ija, wopunzila bake banabwelela. Manje banadabwa kupeza Yesu akamba namuzimayi, koma kulibe anakamba kuti, "nichani chamene ufuna?" kapena kuti "nanga nichani ukamba nauyu muzimayi?"

1
04/28.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 28 Ndipo uyu muzimayi anasiya poto yake yamanzi nakubwelela ku komboni noyenda kuuza bantu kuti, \v 29 "Bwelani, muone mwamuna wamene aniuza zonse zamene ninachita. Uyu sangankhale Kristu, angankhale?" \v 30 Banachokamo mu komboni nakuyenda kwa eve.

1
04/31.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 31 Pantawi yamene ija, bopunzila bake benze kumulimbikisa kuti, "Mupunzisi, dyani." \v 32 Anabayanka kuti, "ine nili nachakudwa chamene inu bonse simuziba olo pang'ono." \v 33 Bopunzila nawo bayamba kufunsana, "kulibe wamene amubwelesela chilichonse chakudwa, nanga bamuletela?"

1
04/34.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 34 Yesu abauza kuti "chakudya changa nikuchita chifunilo cha eve wamene ananituma na kusiliza nchito yake. \v 35 Kodi simumakamba kuti 'kwasala chabe myezi 4 kuti kukolola kuchitike?' Nikuuzani kuti nyamulani manso yanu nakuona minda, chifukwa minda yakonzekela ku kolola naku bweza va mu minda. \v 36 Uyo wamena akolola amalandila malipilo yake, ndipo akututa mbeu ku moyo osasila, kuti ofesa na okolola akondwelee pamozi.

1
04/37.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 37 Ndipo ichi chikamba kuti, 'wina afesa, wina akolola,' nicha zoona. \v 38 Ine nakutumani kuti mukolole minda yamene simunalime. Benangu banasebenza, imwe mwangena chabe munchito yamene banzanu banasebenza kudala.

1
04/39.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 39 Ba Samariya bambili mu muzinda uja banayamba kumukulupilila Yesu chifukwa cha umboni wamene enzekupasa muzimayi uja, kuti, "ananiuza vonse vamene ninachita." \v 40 Pamene ba Samaliya banabwela kwa iye banamupempa kuti ayambe kunkala nabo, naye anankala nabo masiku yabili.

1
04/41.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 41 Na bambili banakulupilila chifukwa cha mau yake. \v 42 Banamuuza muzimayi kuti, "sitinakhulupilile futi chifukwa cha mau yamene watiuza, takhulupilila chifukwa cha mau yamene tazinvelea na mutu watu, ndipo taziba kuti uyu ni mupulumusi wa ziko lonse."

1
04/43.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 43 Patapita masiku yabili, anachokako kuja nakuyenda ku Galileya. \v 44 Chifukwa Yesu wamene anakamba kuti muneneli sibamamupasa ulemu mu ziko yake. \v 45 Pamene anangena mu Galileya, banthu bamu Galileya banamulandila bwino. Benze banaona zonse zamena anachita kuja ku Pwando inankhalila ku Yerusalemu, chifukwa aba banthu nabo benzeko ku Pwando yameni iyi.

1
04/46.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 46 Anabwelelanso ku Kana ku muzinda wa Galileya, kwamene anasandusa manzi vinyo. Ndipo kunali mukulu wina wa ufumu, mwana wake anali odwala ku Kapernaumu. \v 47 Pamene ananvela kuti Yesu achokako ku Yudeya nakubwela ku Galileya, anayenda kwa Yesu nakumupempha kuti abwele achilise uja mwana enze pafuti na kufa.

1
04/48.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 48 Yesu anabauza kuti, "imwe ngati simunaone vizindikilo na vodabwisa, simuzakulupilila." \v 49 Mukulu uyu anamuuza kuti, "Ambuye imwe, bwelani kuno mwamusanga mwana wanga akalibe kufa!" \v 50 Yesu anamuyankha kuti, "Yenda. Mwana wako ali namoyo." Mwamuna uyu anakulupilila zamene anakamba Yesu nakuyenda anayenda.

1
04/51.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 51 Akali kuyenda, ba nchito bake banakumana naye pa njila nakumuuza kuti mwana wako ali namoyo. \v 52 Ndipo anabafunsa ntawi yamene mwana anachilisidwa, nabo banamuyanka kuti "anachilisidwa mailo na ntawi ya wanu koloko ya muzuba."

1
04/53.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 53 Ndipo tate wamwana anazindikila kuti iyo nthawi yenze pamene Yesu anamuuza kuti "mwana wako ali namoyo." Iye na banja yake yonse inakhulupilila mwa Yesu. \v 54 Ichi ndiye chizindikilo chachibili anachita Yesu paneme anachoka ku Yudeya no yenda ku Galileya.

1
04/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 4

1
05/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 5 \v 1 Pamene vinasila ivi penzeli chikondwelero cha Ayuda; ndipo Yesu anayenda ku Yelusalemu. \v 2 Manje mu Yelusalemu pa geti ya mberere, mwenzeli mugodi wa manzi mu chiyebele benzo kaita ati Betesida, yenzeli namakholido yanamutenje yali faivi. \v 3 Mwamene umu munagona banthu bambili odwala, balibe menso, olemala nabozizila mendo kuyembekezela manzi yavundulike. \v 4 Mungelo wa Mulungu enzopitako nthawi zinangu kukavundula manzi, ndipo wamene angenamo pa festi manzi yakali yobvundulika enzo pola matenda yaliyonse yamene anali nayo.

1
05/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Mudala winangu enzeli wodwala kwa zaka 38. \v 6 Pamene Yesu anamuwona kuti aligone, nobwela kuzindikila ati anankhalapo nthawi itali, anabwela amufunsa ati, ufuna kuti upolesewe?

1
05/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Mudala uja odwala anabwela ayankha ati, "Ambuye, nilibe munthu oningenesa mu mugodi ngati manzi yavundulika. Nikafuna kungenamo, winangu abwela angenamo." \v 8 Yesu anabwela akamba ati "Nyamuka, tenga mphasa yako, yenda."

1
05/09.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 9 Pamene apo mudala uja anapola notenga mphasa yake, noyenda. Manje ija siku penzeli pa Sabbatha

1
05/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 So baYuda anabwela akamba namudala wamene anapola ati, "Lelo nipa Sabbatha, sufunika kunyamula mphasa yako." \v 11 Anabwela ayankha ati, "Uja wamene wanipolesa waniuza kuti, 'Tenga mphasa yako yenda."

1
05/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Banabwela bamufusa ati, "Nindani mudala wamene akuuza kuti, 'Tenga mphasa yako, yenda?" \v 13 Koma uja mudala anapolesewa sanamuzibe kuti nindani cifukwa Yesu anayenda yanoziba aliyense, cifukwa penzeli banthu bambili.

1
05/14.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 14 Pamene vinasila ivi, Yesu anamupeza yeve mu Tempele nobwela kumuuza ati, "Ona, wapola manje! Usakacimwe futi, kuti coyipa cocila apo cisakacitike kuli iwe." \v 15 Mudala uja anayenda ndipo anauza baYuda kuti niYesu wamene anamucilisa.

1
05/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Manje cifukwa ca ivi vinthu baYuda banamusausa Yesu, cifukwa cakuti anacita ivi vinthu pa Sabbatha. \v 17 Yesu anabwela abayankha ati, "baTate banga akali kusebenza namanje so, naine nisebenza manje so." \v 18 Cifukwa caici, baYuda anafunisisa kumupaya cifukwacakuti sanapwanye cabe siku la sabatha, koma anaitana Mulungu kunkhala Atate bake eve, nozipanga eve kulingana na Mulungu.

1
05/19.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 19 Yesu anabwela ayankha ati, "Nikuuzani coonadi kuti mwana Mwamuna sangacite vinthu payeve yeka, koma vamene awona baTate bake kucita, vonse vamene baTate acita, mwana mwamuna naive avicita. \v 20 BaTate akonda mwana Mwamuna nakuti bamuwonesa vonse vamene bacita, nakuti bazamuwonesa vinthu vikulu maningi kucila apa ndipo muzadabwa.

1
05/21.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 21 Monga baTate bausha ba kufa nobapasa moyo, namwana Mwamuna apasa moyo kuli aliyense yeve afuna. \v 22 BaTate sibaweluza aliyense, koma apasa mwana Mwamuna kuweluza konse \v 23 kuti bonse balemekeze mwana Mwamuna mwamene alemekezela baTate. Wamene salemekeza mwana Mwamuna salemekeza baTate wake bamene anamutuma

1
05/24.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 24 Kukamba zoonadi, yeve amene anvela mau anga nakukhulupira wamene ananituma anaumoyo wosasila ndipo kulibe ciweluzo, koma wacoka ku imfa wabwela ku moyo

1
05/25.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 25 Kukamba zoona, nthawi ibwela, ndipo yabwela kudala, pamene bakufa bazanvela mau ya mwana Mwamuna wa Mulungu, ndipo amene azanvela azankhala na moyo.

1
05/26.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 26 Monga mwamene baTate banamoyo mulibeve, bapasako futi namwana Mwamuna kuti ankhale namoyo muliyeve, \v 27 nakuti baTate bapasa mwana Mwamuna ulamulilo kuti angapeleke ciweluzo cifukwa nimwana Mwamuna wa munthu.

1
05/28.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 28 Osadabwa naici, ibwela nthawi pamene bonse bali mumanda wazanvela mau yake, \v 29 ndipo bazacoka: baja bamene bacita bwino kukauka kwa moyo, baja bamene bacita zooipa kukauka ku ciwereluziro.

1
05/30.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 30 Siningacite ciliconse paine neka. Pazamene nivela, niweluza, ndipo ciweluzo canga nicolungama cifukwa sinicita mwamene nifunila ine koma nicita kulinga mwamene ananitumila. \v 31 Ngati nizakamba zaine neka, umboni wanga suzankhala wa zoona. \v 32 Koma kuli winangu amene apereka umboni wanga, ndipo niziba kuti umboni wamene apereka pali ine niwazoona.

1
05/33.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 33 Imwe munatuma kwa Yohane, ndipo wapereka umboni wa zoona. \v 34 Koma umboni wamene ndilandila siwucokela kumunthu. Nikamba vonse ivi kuti mupulumuke. \v 35 Yohane anali nyali yoyaka nayowala ndipo imwe munafuna kuti mukodwela mukuwala kwake panthawi ing'ono cabe.

1
05/36.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 36 Koma umboni wamene nili nabo upambana wa Yohane, pa zinchito zamene baTate bananipasa kuti nizikwanilise, zinchito zamene izi zamene nicita, zipeleka umboni kuti baTate bananituma ine. \v 37 BaTate bamene bananituma ine bevebeka bapelekela umboni pazaine. Simunaveleko mau yabo kapena kubona vamenene abonekela. \v 38 Mulibe namau yake yamene yankhala mwa imwe, cifukwa simukhulupilira muli iye wamene iye anatuma.

1
05/39.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 39 Musakila mau aMulungu cifukwa muganiza kuti muliyeve muli umoyo bosasila, ndipo mau yamene aya yapereka umboni pali ine, \v 40 ndipo simufuna kubwela kwa ine kuti mukhale nabo moyo

1
05/41.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 41 Sinilandila mayamiko kuchokela kubanthu, \v 42 koma niziba kuti mulibe cikondi ca Mulungu muli imwe.

1
05/43.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 43 Nabwela muzina la baTate banga, koma simunilandila. Koma winangu akabwela muzinalake mungamulandile. \v 44 Mungakhulupilile bwanji, imwe amene mulandila mayamiko kubanzanu koma simufuna kulandila mayimiko kuchokela kuli Mulungu aliyeka.

1
05/45.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 45 Musanganize kuti ine nizakunenelani kuli baTate. Wamene akunenelani ni Mose, wamene mukhulupilira. \v 46 Ngati mukhulupilira Mose, mungakhulipilire naine cifukwa Mose analemba zaine. \v 47 Ngati simukhulupilira vamene analembe, mungakhulupilire bwanji mu mau yanga?"

1
05/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 5

1
06/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 6 \v 1 Pathapita izi, Yesu anayenda kusidya kwa chimana ca Galileya, chochedwanso chimana ca Tibeliya. \v 2 Gulu likulu la Anthu linamusata iye chifukwa linaona vodabwisa vimene anachita pa wodwala. \v 3 Yeso anakwela ku lupili nakhala pansi ndi wophunzila ake.

1
06/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 ( Tsopano pwando, la Yuda ya pasaka, inali pafupi.) \v 5 Yeso anakweza maso naona gulu likulu la anthu ilikubwela kwa iye, ndipo anati kwa Filipo, "Tizagula kuti buledi kuti tidyese Anthu awa?" \v 6 (Koma Yesu anafunsa Filipo kumuyesa chabe, Chifukwa iye anaziwa camene ayenera kucita.)

1
06/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Filipo anamuyankha nati, " Ngakale makobili miyanda iwili (200) kugula buledi singakwanila aliyense kuti adye ngakale kang'ono chabe. \v 8 M'modzi wa uphunzila ake, Andeleya mbale wa Simoni Petulo anati kuli Yesu, \v 9 "Alipo pano mnyamata aliko na buledi faive na nsomba ziwili, koma izi kulinganiza ndi anthu zingathandize?"

1
06/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Yesu anati, " Awuzeni anthu ankhale pansi." ( Panali uzu wambiri pamalo paja) Amuna amene anakhala pansi enzopitilila pa faive sauzande, (5,000). \v 11 Yesu anathenga buledi atayamika anawapasa waja anankhala pansi Anachitanso chimodzi mozi ndi nsomba, anadya mwakufuna kwawo. \v 12 Pamene banakhuta wonse iye anati kwa ophunzila ake, Tengani vasalapo kuti visaonongeke."

Some files were not shown because too many files have changed in this diff Show More