Sat Dec 28 2019 16:29:50 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Bshop2 2019-12-28 16:29:51 +02:00
parent e9597000a8
commit d8219966c8
7 changed files with 14 additions and 7 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 4 \v 6 Onani, malipilo ya wantchito yalila-malipilo yamene munakana kulipila baja bamene banakolola minda zanu, na kulila kwa bokolola kwa fika mu matu ya Ambuye wa makamo. \v 5 Munankala mozimvesa bwino pa ziko na kusangalalisa moyo zanu. Munainisa mitima zanu kulindila siku ya pwando. Muna weluza naku paya muntu olungama. Sana ku shusheni.
\v 4 Onani, malipilo ya wantchito yalila-malipilo yamene munakana kulipila baja bamene banakolola minda zanu, na kulila kwa bokolola kwa fika mu matu ya Ambuye wa makamo. \v 5 Munankala mozimvesa bwino pa ziko na kusangalalisa moyo zanu. Munainisa mitima zanu kulindila siku ya pwando. \v 6 Muna weluza naku paya muntu olungama. Sana ku shusheni.

View File

@ -1 +1 @@
\v 7 \v 8 Mwa ici nkalani oleza mutima, abale, mpaka kubwela kwa Ambuye. Onani, mulimi ama embekezela vokolola vake vamutengo vochokela mumunda. Amankala oleza mutima kulindila, mpaka pamene alandila mvula yoyamba na yosilizila. Naimwe, chimozo-mozi, nkalani odeka mutima. Limbikisani mitima zanu, chifukwa kubwela kwa Ambuye kuli pafupi.
\v 7 Mwa ici nkalani oleza mutima, abale, mpaka kubwela kwa Ambuye. Onani, mulimi ama embekezela vokolola vake vamutengo vochokela mumunda. Amankala oleza mutima kulindila, mpaka pamene alandila mvula yoyamba na yosilizila. \v 8 Naimwe, chimozo-mozi, nkalani odeka mutima. Limbikisani mitima zanu, chifukwa kubwela kwa Ambuye kuli pafupi.

View File

@ -1 +1 @@
\v 9 \v 10 \v 11 Musadaundaule, abale, wina pali muzake, mwakuti musaweluziwe. Onani, eve oweluza aimilila pa chiseko. Tenganiponi chisanzo, abale, pa kuvutika na kudeka mutima kwa aneneli, bamene bana kamba muzina ya Ambuye. Onani, tima lemekeza baja bana pilila kuti nibo dalisika. Munamvela kulimbikila kwa Yobo, ndipo muziba lingo ya Ambuye, mwamene balili na chikondi komanso ba chifundo.
\v 9 Musadaundaule, abale, wina pali muzake, mwakuti musaweluziwe. Onani, eve oweluza aimilila pa chiseko. \v 10 Tenganiponi chisanzo, abale, pa kuvutika na kudeka mutima kwa aneneli, bamene bana kamba muzina ya Ambuye. \v 11 Onani, tima lemekeza baja bana pilila kuti nibo dalisika. Munamvela kulimbikila kwa Yobo, ndipo muziba lingo ya Ambuye, mwamene balili na chikondi komanso ba chifundo.

View File

@ -1 +1 @@
\v 13 \v 14 \v 15 Nanga pali aliyense pakati panu wamene avutika? Mulekeni apempele. Nanga pali wamene ali na chimwemwe? Mulekeni aimbe nyimbo zama tamando. Nanga pali odwala? Mulekeni aitane bakulu bamu pingo, lekani bamupempelele. Lekani bamu zoze na mafuta muzina ya Ambuye. Pempelo ya chikululupilo izachilisa eve odwala, ndipo Ambuye baza muimya. Ngati anachimwa, Mulungu azamu kululukila.
\v 13 Nanga pali aliyense pakati panu wamene avutika? Mulekeni apempele. \v 14 Nanga pali wamene ali na chimwemwe? Mulekeni aimbe nyimbo zama tamando. Nanga pali odwala? Mulekeni aitane bakulu bamu pingo, lekani bamupempelele. Lekani bamu zoze na mafuta muzina ya Ambuye. \v 15 Pempelo ya chikululupilo izachilisa eve odwala, ndipo Ambuye baza muimya. Ngati anachimwa, Mulungu azamu kululukila.

View File

@ -1 +1 @@
\v 16 \v 17 \v 18 Mwa ici lapani machimo yanu kuli wina na muzake, ndiponso mupempelelane, mwakuti mu polesewe. Pempeleo ya uja olungama niya mpavu mukusebenza kwake. Eliya anali muntu monga ise. Anapempela mokululupira kuti mvula isagwee, ndipo mvula si inagwe paziko zaka zitatu na myezi sikisi. Ndiponso Eliya anapempela kachibili. Kumwamba kunapeleka mvula, na minda inapeleka vipaso vake.
\v 16 Mwa ici lapani machimo yanu kuli wina na muzake, ndiponso mupempelelane, mwakuti mu polesewe. Pempeleo ya uja olungama niya mpavu mukusebenza kwake. \v 17 Eliya anali muntu monga ise. Anapempela mokululupira kuti mvula isagwee, ndipo mvula si inagwe paziko zaka zitatu na myezi sikisi. \v 18 Ndiponso Eliya anapempela kachibili. Kumwamba kunapeleka mvula, na minda inapeleka vipaso vake.

View File

@ -1 +1 @@
\v 19 \v 20 Abale, ngati wina aliyense ataika kucho-onadi, ndiponso winangu amubweza, uja muntu ayenela kuziba kuti aliyense wamene abwezela ochumwa kuchoka mukutaika kwake amupulumusa ku imfa, komanso azavinikila machimo yambili.
\v 19 Abale, ngati wina aliyense ataika kucho-onadi, ndiponso winangu amubweza, \v 20 uja muntu ayenela kuziba kuti aliyense wamene abwezela ochumwa kuchoka mukutaika kwake amupulumusa ku imfa, komanso azavinikila machimo yambili.

View File

@ -76,6 +76,13 @@
"04-13",
"04-15",
"05-title",
"05-01"
"05-01",
"05-04",
"05-07",
"05-09",
"05-12",
"05-13",
"05-16",
"05-19"
]
}