nya-x-nyanja_isa_text_reg/22/25.txt

1 line
181 B
Plaintext

\v 25 Tsiku lomwelo, atero Yehova wa makamu, msomali wokhomedwa wolimba udzagwedezeka, nudzagwetsedwa, ndi kugwa; ndi katundu amene anali pamenepo adzadulidwa, pakuti Yehova wanena.