nya-x-nyanja_isa_text_reg/22/20.txt

1 line
387 B
Plaintext

\v 20 Tsiku lomwelo ndidzayitana mtumiki wanga Eliyakimu mwana wa Hilikiya. \v 21 Ndidzamuveka iye malaya ako, ndi kumveka lamba wako; ndipo ndidzampatsa ulamuliro wako m'dzanja lake. Iye adzakhala atate wa okhala m'Yerusalemu ndi nyumba ya Yuda. \v 22 Ndidzaika kiyi wa nyumba ya Davide paphewa pake. adzatsegula, ndipo palibe amene adzatseke; adzatseka, ndipo palibe amene adzatsegule.