nya-x-nyanja_isa_text_reg/22/15.txt

1 line
244 B
Plaintext

\v 15 Atero Ambuye Yehova wa makamu, Pita kwa woyang'anira uyu, kwa Sebina, woyang'anira nyumba, nunene, \v 16 Udzatani kuno, ndi ndani anakupatsa chilolezo kudzichekera wekha, kudzikonzera manda? Pamtunda ndi kusema malo opumako pathanthwe? '"