nya-x-nyanja_isa_text_reg/22/08.txt

1 line
203 B
Plaintext

\v 8 Anachotsa chitetezo cha Yuda; ndipo udayang'ana tsiku lomwelo kuzida za m'nyumba yachifumu ya nkhalango. \v 9 Mudawona mipata ya mzinda wa David ili yambiri, ndipo mudatunga madzi a dziwe lakumunsi.