Sat Oct 02 2021 11:55:10 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-02 11:55:10 +02:00
parent 01d540c6f9
commit f8c6371f51
5 changed files with 9 additions and 1 deletions

1
61/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Pakuti ine Yehova ndimakonda chilungamo, ndipo ndimadana ndi zauchifwamba ndi chiwawa chosachita chilungamo. Ndidzawabwezera mokhulupirika, ndipo ndidzapangana nawo pangano losatha. \v 9 Mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu a mitundu ina, ndi ana awo pakati pa anthu. Onse amene adzawaona adzawazindikira, kuti ndiwo anthu amene Yehova wawadalitsa.

1
61/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Ndidzakondwera mwa Yehova; mwa Mulungu wanga ndidzakondwera. Pakuti wandiveka ine ndi zovala za chipulumutso; wandiveka ine ndi mwinjiro wachilungamo, monga mkwati amadziveka nduwira, ndiponso monga mkwatibwi azikometsera ndi zibangiri zake. \v 11 Pakuti monga dziko lapansi limeretsa zipatso zake, ndi m'munda momwe umalimamo, momwemonso Ambuye Yehova adzaphukitsa chilungamo ndi chiyamiko pamaso pa amitundu onse.

1
63/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 63 \v 1 Ndani uyu akuchokera ku Edomu, atavala zovala zofiira, wochokera ku Bozira? Ndani uyu, wobvala mwanzeru, nayenda mu ukulu wa mphamvu yake? "Ndine amene, ndiyankhula mwachilungamo, ndi wamphamvu kupulumutsa." \v 2 Chifukwa chiyani zovala zako zili zofiira, ndipo bwanji zikuwoneka ngati ukuponda mphesa moponderamo mphesa?

1
63/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 63

View File

@ -703,6 +703,8 @@
"61-03",
"61-04",
"61-06",
"61-08",
"61-10",
"62-title",
"62-01",
"62-03",
@ -710,6 +712,8 @@
"62-06",
"62-08",
"62-10",
"62-11"
"62-11",
"63-title",
"63-01"
]
}