Sat Oct 02 2021 11:59:11 GMT+0200 (Central Africa Time)
This commit is contained in:
parent
4dc6ca9188
commit
ee8c6108b5
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 10 Koma anapanduka ndi kumvetsa chisoni Mzimu Woyera. Kotero iye anakhala mdani wawo namenyana nawo.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 11 Anthu ake amaganiza za nthawi zakale za Mose. Anati, Ali kuti Mulungu, amene anawaturutsa m'nyanja pamodzi ndi abusa a zoweta zace? Ali kuti Mulungu, amene anaika Mzimu Woyera pakati pao?
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 12 Ali kuti Mulungu, yemwe adapanga mphamvu yake yaulemerero ndi dzanja lamanja la Mose, nagawa madzi pamaso pawo, kuti adzipangire dzina likhale kosatha? \v 13 Ali kuti Mulungu, amene adawatsogolera kuwoloka m'madzi akuya? Monga kavalo akuthamanga pamtunda, sanapunthwe.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 14 Ng'ombe zomwe zikupita kuchigwa, mzimu wa Yehova udawapumitsa. Chifukwa chake mudatsogolera anthu anu, kuti mudzipangire mbiri yakuyamika.
|
|
@ -718,6 +718,10 @@
|
|||
"63-03",
|
||||
"63-05",
|
||||
"63-07",
|
||||
"63-09"
|
||||
"63-09",
|
||||
"63-10",
|
||||
"63-11",
|
||||
"63-12",
|
||||
"63-14"
|
||||
]
|
||||
}
|
Loading…
Reference in New Issue