Fri Oct 01 2021 17:24:33 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-01 17:24:33 +02:00
parent 49eba01ba1
commit cd0c4f6dc1
5 changed files with 7 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 21 \v 22 Koma anthu adangokhala chete osayankha, popeza lamulo la mfumu lidati, "Musamuyankhe." Pamenepo Eliyakimu mwana wa Hilikiya, woyang'anira nyumba yake, Sebina mlembi, ndi Yoa mwana wa Asafu wolemba mbiri, anadza kwa Hezekiya zovala zawo zitang'ambika, namuuza mawu a kazembe wamkulu.
\v 21 Koma anthu adangokhala chete osayankha, popeza lamulo la mfumu lidati, "Musamuyankhe." \v 22 Pamenepo Eliyakimu mwana wa Hilikiya, woyang'anira nyumba yake, Sebina mlembi, ndi Yoa mwana wa Asafu wolemba mbiri, anadza kwa Hezekiya zovala zawo zitang'ambika, namuuza mawu a kazembe wamkulu.

1
37/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 37 \v 1 Ndipo kunali, atamva mfumu Hezekiya, anang'amba zobvala zace, navala ciguduli, nalowa m'nyumba ya Yehova. \v 2 Ndipo anatuma Eliyakimu, woyang'anira nyumba, ndi Sebina mlembi, ndi akulu a ansembe, onse atavala ziguduli, kwa mneneri Yesaya mwana wa Amozi.

1
37/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 \v 4 Nati kwa iye, Hezekiya anena, Lero ndilo tsiku losautsa, lodzudzula, ndi lotonza, monga ngati mwana ali pafupi kubadwa, koma amake alibe mphamvu yakubala mwana wao. Mulungu wanu adzamva mawu a kazembe wamkulu, amene mbuye wake mfumu ya Asuri yamtuma kunyoza Mulungu wamoyo, nadzadzudzula mawu amene Yehova Mulungu wanu wamva. . ""

1
37/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 37

View File

@ -417,6 +417,9 @@
"36-13",
"36-16",
"36-18",
"36-21",
"37-title",
"37-01",
"38-title",
"38-01",
"38-04",