Sat Oct 02 2021 14:55:04 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-02 14:55:05 +02:00
parent 05e29177d7
commit b81367db9f
3 changed files with 5 additions and 1 deletions

1
66/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 Pakuti monga m'mwamba mwatsopano ndi dziko lapansi latsopano limene ndidzapanga zidzakhala pamaso panga, ati Yehova, chomwechonso mbewu yanu idzatsalira, ndipo dzina lanu lidzakhalabe. \v 23 Kuyambira mwezi umodzi kufikira tsiku lina, ndipo kuyambira Sabata lina kufikira tsiku linzace, anthu onse adzadza kudzandigwadira ine, ati Yehova.

1
66/24.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 24 Adzatuluka kukawona mitembo ya anthu omwe andipandukira ine, chifukwa mphutsi zomwe zimawadya sidzafa, ndipo moto umene udzawonongedwe sudzazimitsidwa; ndipo chidzakhala chonyansa kwa anthu onse."

View File

@ -763,6 +763,8 @@
"66-15",
"66-17",
"66-18",
"66-20"
"66-20",
"66-22",
"66-24"
]
}