Sat Oct 02 2021 12:05:16 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-02 12:05:17 +02:00
parent 20844c2c37
commit a096a3a99c
5 changed files with 9 additions and 1 deletions

1
64/06.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 6 Pakuti tonse takhala ngati wodetsedwa, ndipo ntchito zathu zonse zolungama zili ngati nsanza yakusamba. Tonse tafota ngati masamba; mphulupulu zathu zitiuluza monga mphepo. \v 7 Palibe amene amayitana dzina lanu, amene amayesetsa kukugwirani. Pakuti mwatibisira nkhope yanu, ndipo mwatitayitsa m'manja a mphulupulu zathu.

1
64/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Komatu Yehova, inu ndinu atate wathu; ndife dongo. Inu ndinu wotiumba wathu; ndipo ife tonse ndife ntchito ya dzanja lanu. \v 9 Musakwiye kwambiri, Yehova, ndipo musakumbukire zolakwa zathu nthawi zonse. Chonde yang'anani pa ife tonse, anthu anu

1
64/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Midzi yanu yopatulika yasanduka chipululu; Ziyoni wasanduka chipululu, ndi Yerusalemu bwinja. \v 11 Kachisi wathu woyera ndi wokongola, pomwe makolo athu adakutamandani, wawonongedwa ndi moto, ndipo zonse zomwe zidakondedwa zawonongedwa. \v 12 Nanga ungabebe bwanji, Yehova? Kodi mungakhale bwanji chete ndikupitiliza kutichititsa manyazi? "

1
65/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 65

View File

@ -729,6 +729,10 @@
"64-title",
"64-01",
"64-03",
"64-05"
"64-05",
"64-06",
"64-08",
"64-10",
"65-title"
]
}