Fri Oct 01 2021 16:50:39 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-01 16:50:39 +02:00
parent b97098148b
commit 84162b54dd
4 changed files with 6 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 7 \v 8 Zidzakhala ngati loto, masomphenya a usiku: Gulu lalikulu la mitundu yonse lidzamenyana ndi Arieli ndi malo ake achitetezo. Iwo adzamuukira ndi malinga ake kuti amuthamange. Zidzakhala ngati munthu wanjala alota kuti akudya, koma akadzuka, m'mimba mwake mulibe kanthu. Zidzakhala ngati munthu waludzu atalota kuti akumwa, koma iye podzuka, akukomoka, ndi ludzu lake losatha. Inde, chomwechonso chiwerengero cha mayiko omwe adzamenyane ndi Phiri la Ziyoni.
\v 7 Zidzakhala ngati loto, masomphenya a usiku: Gulu lalikulu la mitundu yonse lidzamenyana ndi Arieli ndi malo ake achitetezo. Iwo adzamuukira ndi malinga ake kuti amuthamange. \v 8 Zidzakhala ngati munthu wanjala alota kuti akudya, koma akadzuka, m'mimba mwake mulibe kanthu. Zidzakhala ngati munthu waludzu atalota kuti akumwa, koma iye podzuka, akukomoka, ndi ludzu lake losatha. Inde, chomwechonso chiwerengero cha mayiko omwe adzamenyane ndi Phiri la Ziyoni.

1
31/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 31 \v 1 Tsoka kwa iwo amene apita ku Aigupto kukathandizidwa ndi kudalira akavalo, ndi kukhulupirira magaleta (pakuti achulukadi) ndi apakavalo; Koma alibe nkhawa ndi Woyera wa Israeli, komanso safuna Yehova! \v 2 Komabe iye ndi wanzeru, ndipo adzabweretsa tsoka ndipo sadzabweza mawu ake. Adzaukira nyumba yoyipa, ndi otsutsana nawo amene achimwa.

1
31/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 31

View File

@ -334,6 +334,7 @@
"29-01",
"29-03",
"29-05",
"29-07",
"29-09",
"29-11",
"29-13",
@ -362,6 +363,8 @@
"30-30",
"30-31",
"30-33",
"31-title",
"31-01",
"32-title",
"32-01",
"32-04",