Fri Oct 01 2021 17:06:30 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-01 17:06:31 +02:00
parent b2b2b94328
commit 62923a628f
6 changed files with 10 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 5 \v 7 Monga mbalame zouluka, momwemo Yehova wa makamu adzatchinjiriza Yerusalemu; adzateteza ndi kupulumutsa pamene adutsa ndi kuisunga. \v 6 Bwererani kwa iye amene mwapatuka kwambiri, inu ana a Israeli. Pakuti tsiku lomwelo adzachotsa yense mafano ake a siliva, ndi mafano ake a golidi, amene manja anu anachimwa
\v 5 Monga mbalame zouluka, momwemo Yehova wa makamu adzatchinjiriza Yerusalemu; adzateteza ndi kupulumutsa pamene adutsa ndi kuisunga. \v 6 Bwererani kwa iye amene mwapatuka kwambiri, inu ana a Israeli. \v 7 Pakuti tsiku lomwelo adzachotsa yense mafano ake a siliva, ndi mafano ake a golidi, amene manja anu anachimwa

1
31/08.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 8 Asuri adzaphedwa ndi lupanga; lupanga losagwira munthu lidzamutentha. Iye adzathawa lupanga, ndipo anyamata ake adzawakakamiza kugwira ntchito yolemetsa. \v 9 Iwo adzataya chidaliro chonse chifukwa cha mantha, ndipo akalonga ake adzaopa pamaso pa mbendera ya Yehova, ati Yehova, amene moto wake uli m'Ziyoni, ndi woyatsa moto ali m'Yerusalemu.

1
34/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 34 \v 1 Yandikirani, amitundu inu, mumve; tamverani, anthu inu! Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ziyenera kumvera, dziko lapansi ndi zinthu zonse zochokera mmenemo. \v 2 Pakuti Yehova wakwiyira amitundu onse, ndipo akwiyira magulu awo onse ankhondo; wawawonongeratu, wawapereka kukaphedwa.

1
34/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Mitembo ya akufa awo idzaponyedwa kunja. Kununkha kwa mitembo kudzakhala paliponse; ndipo mapiri adzakhetsa magazi awo. \v 4 Nyenyezi zonse zakumwamba zidzatha, ndipo thambo lidzakulungidwa ngati mpukutu; ndipo nyenyezi zawo zonse zidzakomoka, monga tsamba lothothoka pa mpesa, ndi nkhuyu zofesa pa mkuyu.

1
34/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 34

View File

@ -367,6 +367,8 @@
"31-01",
"31-03",
"31-04",
"31-05",
"31-08",
"32-title",
"32-01",
"32-04",
@ -390,6 +392,9 @@
"33-20",
"33-22",
"33-23",
"34-title",
"34-01",
"34-03",
"38-title",
"38-01",
"38-04",