diff --git a/22/20.txt b/22/20.txt new file mode 100644 index 0000000..437b26c --- /dev/null +++ b/22/20.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 20 Tsiku lomwelo ndidzayitana mtumiki wanga Eliyakimu mwana wa Hilikiya. \v 21 Ndidzamuveka iye malaya ako, ndi kumveka lamba wako; ndipo ndidzampatsa ulamuliro wako m'dzanja lake. Iye adzakhala atate wa okhala m'Yerusalemu ndi nyumba ya Yuda. \v 22 Ndidzaika kiyi wa nyumba ya Davide paphewa pake. adzatsegula, ndipo palibe amene adzatseke; adzatseka, ndipo palibe amene adzatsegule. \ No newline at end of file diff --git a/22/23.txt b/22/23.txt new file mode 100644 index 0000000..42e314e --- /dev/null +++ b/22/23.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 23 Ndidzamukhomerera, ngati msomali pamalo okhazikika, ndipo iye adzakhala mpando wa ulemu m'nyumba ya atate wake. \v 24 Adzapachika pa iye ulemu wonse wam'nyumba ya abambo ake, ana ndi zidzukulu, chidebe chilichonse chaching'ono kuyambira pamakapu mpaka mitsuko yonse. \ No newline at end of file diff --git a/22/25.txt b/22/25.txt new file mode 100644 index 0000000..1ee6fa1 --- /dev/null +++ b/22/25.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 25 Tsiku lomwelo, atero Yehova wa makamu, msomali wokhomedwa wolimba udzagwedezeka, nudzagwetsedwa, ndi kugwa; \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index 09e8812..92167be 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -261,6 +261,8 @@ "22-12", "22-15", "22-17", + "22-20", + "22-23", "24-title", "24-01", "24-03",