Fri Oct 01 2021 17:10:31 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-01 17:10:31 +02:00
parent f3b799581c
commit 438020aeb1
5 changed files with 8 additions and 0 deletions

1
34/13.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 13 Minga idzadzaza nyumba zake zachifumu, lunguzi ndi mitula m'malo mwake; Udzakhala mokhalamo mimbulu, malo a nthiwatiwa. \v 14 Nyama zakutchire ndi afisi adzakumana kumeneko, ndipo mbuzi zamtchire zidzalira wina ndi mnzake. Nyama zakutchire zimakhazikika kumeneko ndikupeza malo ampumulo. \v 15 Ziwombankhanga zimapanga zisa, kuikira mazira ndi kuwaswa, zimaswa ndi kuteteza ana awo. Inde, akamba azikasonkhana pamodzi, yense ndi mnzake.

1
34/16.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 16 Fufuzani mumpukutu wa Yehova; palibe imodzi mwa izi idzasowa. Palibe amene adzasowe wokwatirana naye; pakuti m'kamwa mwache adalamulira, ndipo mzimu wake udawasonkhanitsa. \v 17 Wachita maere kuti apeze malo awo, ndipo dzanja lake lawayeza ndi chingwe. Iwo adzakhala nazo mpaka kalekale. adzakhala kumeneko ku mibadwomibadwo.

1
35/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 35 \v 1 Chipululu ndi Araba zidzakondwera; ndipo chipululu chidzakondwera ndi kuchita maluwa. Monga duwa, \v 2 lidzaphuka mochuluka ndi kusangalala ndi chisangalalo ndi kuyimba; lidzapatsidwa ulemerero wa Lebano, ndi ukuru wa Karimeli ndi Sharoni; adzaona ulemerero wa Yehova, ndi ukulu wa Mulungu wathu;

1
35/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 35

View File

@ -399,6 +399,10 @@
"34-07",
"34-08",
"34-11",
"34-13",
"34-16",
"35-title",
"35-01",
"38-title",
"38-01",
"38-04",