Mon Oct 04 2021 13:05:16 GMT+0200 (Central Africa Time)
This commit is contained in:
parent
98d90345b0
commit
337ad79021
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 3 Pakuti manja anu ali ndi magazi ndi zala zanu ndi uchimo. Milomo yanu imanena mabodza ndipo lilime lanu limayankhula zoyipa. \v 4 Palibe amene adzaitane mwachilungamo, ndipo palibe womteteza m'choonadi. Iwo amakhulupirira mawu opanda pake ndipo amanama. amatenga pakati n mavuto amabereka tchimo.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 5 Amaswa mazira a njoka yapoizoni ndipo amaluka ukonde wa kangaude. Aliyense amene adya mazira ake amafa, ndipo dzira likaphwanyidwa, limaswedwa ndi njoka yapoizoni. \v 6 Ukonde wawo sungagwiritsidwe ntchito ngati zovala, kapena kudziphimba ndi ntchito zawo. Ntchito zawo ndi ntchito zauchimo, ndipo ziwawa zili m'manja mwawo.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 7 Mapazi awo athamangira zoipa, ndipo amathamangira kukakhetsa magazi osalakwa. Malingaliro awo ndi malingaliro a tchimo; chiwawa ndi chiwonongeko ndizo njira zawo. \v 8 Njira yamtendere sadziwa, ndipo palibe chilungamo m'mayendedwe awo. Akuyenda m'njira zopotoka; amene amayenda m'njira izi sadziwa mtendere.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 9 Chifukwa chake chilungamo chili kutali ndi ife, ndipo chilungamo sichitifikira. Tikuyembekezera kuwala, koma tiona mdima; timayembekezera kuwala, koma timayenda mumdima. \v 10 Timapapasa khoma ngati akhungu, ngati iwo osaona; Timapunthwa masana monga ngati m'bandakucha; mwa amphamvu tili ngati akufa.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 11 Tifuula ngati zimbalangondo, ndi kubuma ngati nkhunda; tiyembekezera chiweruzo, koma palibe; zopulumutsa, koma zili kutali ndi ife.
|
|
@ -702,6 +702,10 @@
|
|||
"58-14",
|
||||
"59-title",
|
||||
"59-01",
|
||||
"59-03",
|
||||
"59-05",
|
||||
"59-07",
|
||||
"59-09",
|
||||
"60-title",
|
||||
"60-01",
|
||||
"60-02",
|
||||
|
|
Loading…
Reference in New Issue