Fri Oct 01 2021 15:15:11 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-01 15:15:12 +02:00
parent c8709bc414
commit 3205ee052d
7 changed files with 10 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 2 \v 3 Imvani, miyamba, mvuwe, dziko lapansi; pakuti Yehova wanena, Ndinalera bwino ndi kulera ana, koma iwo andipandukira. Ng'ombeyo idadziwa mwini wake, ndi bulu amadziwa mbiya yake, koma Israyeli samadziwa, Israyeli samazindikira.
\v 2 Imvani, miyamba, mvuwe, dziko lapansi; pakuti Yehova wanena, Ndinalera bwino ndi kulera ana, koma iwo andipandukira. \v 3 Ng'ombeyo idadziwa mwini wake, ndi bulu amadziwa mbiya yake, koma Israyeli samadziwa, Israyeli samazindikira.

1
02/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 2 \v 1 Zinthu zimene Yesaya mwana wa Amozi anaziona m'masomphenya, zokhudza Yuda ndi Yerusalemu. \v 2 Kudzakhala m'masiku otsiriza kuti phiri la nyumba ya Yehova lidzakhazikika monga phiri lalitali kwambiri, ndipo lidzakwezedwa pamwamba pa zitunda, ndipo mafuko onse adzakhamukira kumeneko.

1
02/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Anthu ambiri adzabwera nati, Tiyeni tikwere kunka kuphiri la Yehova, ku nyumba ya Mulungu wa Yakobo, kuti atiphunzitse zina mwa njira zake, ndipo tidzayenda m'mayendedwe ake. Pakuti m'Ziyoni mudzatuluka chilamulo, ndi mawu a Yehova kuchokera ku Yerusalemu.

1
02/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Iye adzaweruza pakati pa akunja, nadzaweruza mitundu yambiri ya anthu; iwo adzasula malupanga awo akhale zolimira, ndi nthungo zawo zikhale anangwape; mtundu sudzanyamula lupanga kumenyana ndi mtundu wina, ndipo sadzaphunziranso nkhondo.

1
02/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
A nyumba ya Yakobo, tiyeni, tiyende m'kuwala kwa Yehova. 6Pakuti mwataya anthu anu, nyumba ya Yakobo, popeza adzala ndi miyambo ya kum'mawa, ndipo aombeza ula monga Afilisti, ndipo agwirana chanza ndi ana a mlendo.

1
02/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 2

View File

@ -40,6 +40,7 @@
"front-title",
"01-title",
"01-01",
"01-02",
"01-04",
"01-05",
"01-07",
@ -57,6 +58,9 @@
"01-27",
"01-29",
"01-31",
"02-title",
"02-01",
"02-03",
"04-01",
"04-03",
"04-05",