Fri Oct 01 2021 17:14:31 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-01 17:14:31 +02:00
parent 20b01113b2
commit 0f2eafadcd
5 changed files with 8 additions and 0 deletions

1
35/10.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 10 Oomboledwa a Yehova adzabwera nadzafika ku Ziyoni akuyimba, ndi chimwemwe chosatha chidzakhala pa mitu yawo; kukondwa ndi chimwemwe zidzawapeza; chisoni ndi kuusa moyo kudzachoka.

1
36/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 36 \v 1 M'chaka cha 14 cha Mfumu Hezekiya, Senakeribu mfumu ya Asuri anaukira mizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri. \v 2 Pamenepo mfumu ya Asuri inatumiza kazembe wamkulu wa nkhondo kuchokera ku Lakisi kupita ku Yerusalemu kwa Mfumu Hezekiya ndi gulu lankhondo lalikulu. Adayandikira ngalande ya dziwe lakumtunda, panjira yayikulu yopita kumunda wa ochapa zovala, ndipo adayima pamenepo. \v 3 Aisraeli amene anatuluka mu mzindawo kukayankhula nawo anali Eliyakimu, mwana wa Hilikiya, woyang palaceanira nyumba yachifumu, Sebina mlembi wa mfumu, ndi Yowa mwana wa Asafu, amene analemba malamulo a boma.

1
36/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Mkulu wa asilikaliyo anawawuza kuti, "Uzani Hezekiya kuti mfumu yayikulu, mfumu ya Asuri, yanena kuti, 'Kodi ukudalira chiyani? \v 5 Mukungonena mawu opanda pake, kunena kuti pali uphungu ndi mphamvu zankhondo. wakhulupirira ndani wakupatsa iwe mphamvu kuti undiwukire?

1
36/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 36

View File

@ -406,6 +406,10 @@
"35-03",
"35-05",
"35-08",
"35-10",
"36-title",
"36-01",
"36-04",
"38-title",
"38-01",
"38-04",