Sat Oct 02 2021 08:37:13 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-02 08:37:14 +02:00
parent e07eb97472
commit 0bb1694ad4
5 changed files with 9 additions and 0 deletions

1
46/12.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 12 Mverani Ine, anthu amitima yanu, amene mwachita zosalungama. \v 13 Ndikubweretsa chilungamo changa pafupi; sichiri patali, ndipo chipulumutso changa sichidikira; ndipo ndidzapulumutsa Ziyoni, ndi kukongola kwanga kwa Israyeli.

1
47/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 47 \v 1 Tsika ukhale m'fumbi, namwaliwe, mwana wamkazi wa Babulo; khala pansi wopanda mpando wachifumu, mwana wamkazi wa Akasidi. Simudzatchedwanso ofooka komanso osakhwima. \v 2 Tenga mphero, nupere ufa; chotsa chophimba chako, vula chovala chako chotseguka, vula miyendo yako, uwoloke mitsinje.

1
47/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Umaliseche wako udzaululika, inde manyazi ako adzawoneka; ndidzabwezera, sindidzasunga munthu. \v 4 Wotiwombola, Yehova wa makamu dzina lake, Woyera wa Israyeli. \v 5 Khala chete, nulowe mumdima, mwana wamkazi wa Akasidi; chifukwa sudzatchedwanso mfumukazi ya maufumu.

1
47/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 47

View File

@ -562,6 +562,11 @@
"46-05",
"46-07",
"46-08",
"46-10",
"46-12",
"47-title",
"47-01",
"47-03",
"49-title",
"49-01",
"49-03",