Fri Oct 01 2021 15:49:15 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-01 15:49:15 +02:00
parent d222f92468
commit 02a4940ce4
3 changed files with 4 additions and 0 deletions

1
09/18.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 18 Kuipa kuyaka ngati moto; umadya minga ndi minga; imaotcha ngakhale nkhalango, zomwe zimatuluka utsi. \v 19 Ndi ukali wa Yehova wa makamu dziko latenthedwa, ndipo anthu akunga nkhuni. Palibe munthu akumvera chisoni mbale wake.

1
09/20.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 20 Adzagwira dzanja lamanja, nadzamva njala; adzadya chakudya kumanzere koma osakhuta. Aliyense adzadya nyama ya mkono wake. \v 21 Manase adzadya Efraimu, ndi Efraimu adzadya Manase; Iwo onse pamodzi adzaukira Yuda. Mu zinthu zonsezi, mkwiyo wake sutha; m'malo mwake, dzanja lake lidakali lotambasulidwa.

View File

@ -141,6 +141,8 @@
"09-11",
"09-13",
"09-16",
"09-18",
"09-20",
"10-title",
"10-01",
"10-03",