Wed Dec 25 2019 15:08:14 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-12-25 15:08:14 +02:00
parent b11ceb6c64
commit 280ec8ba49
10 changed files with 20 additions and 9 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 4 \v 5 Eve anankala mukulu kuli bangelo monga zina yamene anapasiwa kunkala yopambana kuchila yao, nibandani bangelo bamene Mulungu anauza kuti ndiwe mwana wanga, "lelo nankala Tate wako?" Kapena nindani m'ngelo wamene Mulungu anauza kuti, "Nizankala Tate kwa eve nakuti azankala mwana kuli ine?"
\v 4 Eve anankala mukulu kuli bangelo monga zina yamene anapasiwa kunkala yopambana kuchila yao, nibandani bangelo bamene Mulungu anauza kuti ndiwe mwana wanga, "lelo nankala Tate wako?" \v 5 Kapena nindani m'ngelo wamene Mulungu anauza kuti, "Nizankala Tate kwa eve nakuti azankala mwana kuli ine?"

View File

@ -1 +1 @@
\v 6 \v 7 Kumo futi pamene Mulungu abwelesa mwana oyamba mu ziko, akamba kuti, "Bonse bangelo ba Mulungu bafunika kumupembeza. Pali bangelo akamba kuti, "Ndiye Wamene alenga bangelo bake kunkala chimbili-mbili."
\v 6 Kumo futi pamene Mulungu abwelesa mwana oyamba mu ziko, akamba kuti, "Bonse bangelo ba Mulungu bafunika kumupembeza. \v 7 Pali bangelo akamba kuti, "Ndiye Wamene alenga bangelo bake kunkala chimbili-mbili."

View File

@ -1 +1 @@
\v 8 \v 9 Koma kuli Mwana wake akamba kuti, "Mupando Wako wachifumu, Mulungu, ni wamuyayaya. Ndodo ya ufumu wako ni ndodo ya yachilungamo. Wakonda chilungamo ndipo wazonda kusakonka lamulo. Mwa ici, Mulungu Wako, akuzoza na mafuta ya chimwemwe kuchilapo banzako.
\v 8 Koma kuli Mwana wake akamba kuti, "Mupando Wako wachifumu, Mulungu, ni wamuyayaya. Ndodo ya ufumu wako ni ndodo ya yachilungamo. \v 9 Wakonda chilungamo ndipo wazonda kusakonka lamulo. Mwa ici, Mulungu Wako, akuzoza na mafuta ya chimwemwe kuchilapo banzako.

View File

@ -1 +1 @@
\v 10 \v 11 \v 12 Poyamba, Ambuye, munaika maziko ya chalo cha pansi. Kumwamba ni chilengedwe cha manja Yanu. Bazaonongeka, koma imwe muzapitiliza. Bonse bazasila monga chovala. Muzakavipeteka monga chi koti, ndipo vizachinjiwa monga chovala. Koma imwe mukali chimozi-mozi, ndiponso ma siku yanu siyasila.
\v 10 Poyamba, Ambuye, munaika maziko ya chalo cha pansi. Kumwamba ni chilengedwe cha manja Yanu. \v 11 Bazaonongeka, koma imwe muzapitiliza. Bonse bazasila monga chovala. \v 12 Muzakavipeteka monga chi koti, ndipo vizachinjiwa monga chovala. Koma imwe mukali chimozi-mozi, ndiponso ma siku yanu siyasila.

View File

@ -1 +1 @@
\v 13 \v 14 Nindani m'ngelo wamene Mulungu anauza pantawi iliyonse kuti, "Nkala ku kwanja yanga yamanja mpaka nilenge badani bako kunkala mupando boikapo mendo yako?" Kansi bangelo simizimu zotumikila, ndipo botumiwa kukasamalila bonse baja bazalandila chipulumuso?
\v 13 Nindani m'ngelo wamene Mulungu anauza pantawi iliyonse kuti, "Nkala ku kwanja yanga yamanja mpaka nilenge badani bako kunkala mupando boikapo mendo yako?" \v 14 Kansi bangelo simizimu zotumikila, ndipo botumiwa kukasamalila bonse baja bazalandila chipulumuso?

1
02/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 2

View File

@ -1 +1 @@
\c 11 \v 1 \v 2 \v 3 Manje chikhulupililo nikunkhala wa simikizila pa vinthu vamene \v 3 muyembekeza, zosaoneka. Chifukwa ca ici makolo batu anakhala ba chikulupililo. Mwa chikulupililo timvesesa kuti chalo china lengewa na wamu Mulungu mo lamulila, kuti manje vo oneka vinapangiwa mopanda zoneka.
\c 11 \v 1 Manje chikhulupililo nikunkhala wa simikizila pa vinthu vamene muyembekeza, zosaoneka. \v 2 Chifukwa ca ici makolo batu anakhala ba chikulupililo. \v 3 Mwa chikulupililo timvesesa kuti chalo china lengewa na wamu Mulungu mo lamulila, kuti manje vo oneka vinapangiwa mopanda zoneka.

View File

@ -1 +1 @@
\v 5 \v 6 Ndi mwa chikulupililo kuti Enoki anatengewa kumwamba kuti asaone infa. " Akalibe kutengewa ku mwamba anachitila umboni kuti anakondwelesa Mulungu. Manje mopanda chikulupililo na chovuta, kukondwelesa, ise. Chifukwa ca ici cho chofunikila kuti aliyense amene abwela kwa Mulungu akhale na chikulupililo kuti aliko kuti ni eve apasa mpaso kwa eve amene amusakila.
\v 5 Ndi mwa chikulupililo kuti Enoki anatengewa kumwamba kuti asaone infa. " Akalibe kutengewa ku mwamba anachitila umboni kuti anakondwelesa Mulungu. \v 6 Manje mopanda chikulupililo na chovuta, kukondwelesa, ise. Chifukwa ca ici cho chofunikila kuti aliyense amene abwela kwa Mulungu akhale na chikulupililo kuti aliko kuti ni eve apasa mpaso kwa eve amene amusakila.

View File

@ -1 +1 @@
\v 8 \v 9 \v 10 ndi chikulupililo kuti Abuham, pamene anayitaniwa, anamvelela napita kunja kwa mene anali ku pasiwa vinthu cholowa. Anayenda kunja, osaziba kumene anati apite. Ndi mwa chikulupililo kuti anakhala mdziko ionjezewa imene sinali ya kwao. Anakhala mu msasa na Isaki na Yokobo, Abale ana achiyembe chimodzi. Pakuti analikuyembekezela kuona mdzinda wamaziko opanga naku mangiwa na Mulungu.
\v 8 \v 10 ndi chikulupililo kuti Abuham, pamene anayitaniwa, anamvelela napita kunja kwa mene anali ku pasiwa vinthu cholowa. Anayenda kunja, osaziba kumene anati apite. \v 9 Ndi mwa chikulupililo kuti anakhala mdziko ionjezewa imene sinali ya kwao. Anakhala mu msasa na Isaki na Yokobo, Abale ana achiyembe chimodzi. Pakuti analikuyembekezela kuona mdzinda wamaziko opanga naku mangiwa na Mulungu.

View File

@ -39,6 +39,16 @@
"front-title",
"01-title",
"01-01",
"11-title"
"01-04",
"01-06",
"01-08",
"01-10",
"01-13",
"02-title",
"11-title",
"11-01",
"11-04",
"11-05",
"11-07"
]
}