Wed Dec 25 2019 15:12:14 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2019-12-25 15:12:15 +02:00
parent 5f863c894f
commit 087fe7f9c0
5 changed files with 9 additions and 5 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 32 \v 33 \v 34 Nanga nivichani ningakambe apa, pakuti nthawi sindilola ngati ningakambe za Gedioni,Barak, Samson, Jefitali,Davidi, Samuel ndiponso kunena pa aza aneneri. Zinali mwa chikulupililo anali agonjesa maufumu, anacita ku lungamo, ndipo analandila malonjezo. Analekesa pakamwa pa mkango, a zimya mphamvu ya mulilo, bataba kunolakwa lupanga, anacilisiwa ku matenda yonse, anankhala amphamvu mu nkondo, ana gonjeza adani alendo ankhondo.
\v 32 Nanga nivichani ningakambe apa, pakuti nthawi sindilola ngati ningakambe za Gedioni,Barak, Samson, Jefitali,Davidi, Samuel ndiponso kunena pa aza aneneri. \v 33 Zinali mwa chikulupililo anali agonjesa maufumu, anacita ku lungamo, ndipo analandila malonjezo. Analekesa pakamwa pa mkango, \v 34 a zimya mphamvu ya mulilo, bataba kunolakwa lupanga, anacilisiwa ku matenda yonse, anankhala amphamvu mu nkondo, ana gonjeza adani alendo ankhondo.

View File

@ -1 +1 @@
\v 35 \v 36 \v 37 \v 38 Azimai analandila ba kufa kupitila mu ciukiso. Ena ana menyewa,osalandila kumasuka, kuti amilile mphamvu ya ociukiso yabwino, kumangikwa naku ponyewa mndende.Ana ponyewa miala. anadulilwa pa wili. Anapayiwa nalupanga. Anayenda mu vikumba va nkhosa na mbuzi. Anali anthu ofuma fuma, ndiku nzunzika, anabvutisiwa. Dziko silinali ya bwino kwa eve. Anali kuyenda-yenda mu chipululu namu mapili,godi namu mgodi.
\v 35 Azimai analandila ba kufa kupitila mu ciukiso. \v 36 Ena ana menyewa,osalandila kumasuka, kuti amilile mphamvu ya ociukiso yabwino, kumangikwa naku ponyewa mndende. \v 37 Ena ponyewa miala. anadulilwa pa wili. Anapayiwa nalupanga. Anayenda mu vikumba va nkhosa na mbuzi. Anali anthu ofuma fuma, ndiku nzunzika, anabvutisiwa. \v 38 Dziko silinali ya bwino kwa eve. Anali kuyenda-yenda mu chipululu namu mapili,godi namu mgodi.

View File

@ -1 +1 @@
\v 39 \v 40 Ngankhale kuti anthu awa anali ovomelekezewa na Mulungu chifukwa cha chikulupililo, sana landile lonjezo. Mulungu anakonzelatu za bwino za ise, kuti kulibe ise, ziko ife sizizakhala zo fikapo.
\v 39 Ngankhale kuti anthu awa anali ovomelekezewa na Mulungu chifukwa cha chikulupililo, sana landile lonjezo. \v 40 Mulungu anakonzelatu za bwino za ise, kuti kulibe ise, ziko ife sizizakhala zo fikapo.

View File

@ -1 +1 @@
\c 12 \v 1 \v 2 \v 3 Chifukwa cha ici, ifenso, popeza tizinguluziwamanthu ambili ochitila umboni, tileke colemagiliyonse cimatipele kucimo, mwamsanga, tiyeni tamanga na kupilila luwilo yamene ali pa sogolo pa ise.Tiyene tiyanganile kwa Yesu, anayamba wokonza bwino chikulupililo .pakuti cimwemwe cinaikika pa iye, ana pilika pa mtanda, anacitisiwa manyazi anakhala pa zanja la mpando wa cifumu wa Mulungu. Tsopano ganizani pa eve, amene apilila kususana kocokela kwa ocimwa kwaeve yeka, kuti musabvutike naku teya mtima.
\c 12 \v 1 \v 3 Chifukwa cha ici, ifenso, popeza tizinguluziwamanthu ambili ochitila umboni, tileke colemagiliyonse cimatipele kucimo, mwamsanga, tiyeni tamanga na kupilila luwilo yamene ali pa sogolo pa \v 2 ise. Tiyene tiyanganile kwa Yesu, anayamba wokonza bwino chikulupililo .pakuti cimwemwe cinaikika pa iye, ana pilika pa mtanda, anacitisiwa manyazi anakhala pa zanja la mpando wa cifumu wa Mulungu. Tsopano ganizani pa eve, amene apilila kususana kocokela kwa ocimwa kwaeve yeka, kuti musabvutike naku teya mtima.

View File

@ -58,6 +58,10 @@
"11-20",
"11-23",
"11-27",
"11-29"
"11-29",
"11-32",
"11-35",
"11-39",
"12-title"
]
}