1 line
311 B
Plaintext
1 line
311 B
Plaintext
\v 17 Aba uza wa nchito woyamba kuti, pamene Esau mubale wanga akumana naiwe na kukufunsa, kukamba, ili kumbali yandani? Upita kuti? ni nyama zandani izi zili kusogolo kwako? \v 18 Ndipo uza kamba kuti, 'ndiwa nchito wako Yokobo ndi mphaso yatumi ziwa kuli bwana wanga Esau. Ona, naye alikubwela mumbuyo mwathu. |