nya-x-nyanja_gen_text_reg/38/29.txt

1 line
246 B
Plaintext

\v 29 Koma pamene ana bweza kwanja, ndipo, Onani, bale wake anayambilila kuchoka. Wobalisa anakamba kuti, "Mwewachokela!" Ndipo bana mwitana kuti Perezi. \v 30 Bale wake anachika, anali naka ntambo ka redi pa kwanja, ndipo bana mwitana kuti Zera.