nya-x-nyanja_gen_text_reg/43/28.txt

1 line
356 B
Plaintext

\v 28 Bana kamba, " Wachito wanu atate batu bali bwino akali namoyo." Ndipo anamu gwadila kumu chitila ulemu. \v 29 Pamene ana nyamula menso yake ana ona Benjamini mu bale wake, mwana waba mao make mwamuna. Ndipo ana kamba, " Uyu dye mungono wake wamene una kambapo kuline?" Ndipo ana kamba. " Leka Mulungu aku chitile chisomo kwa iwe mwana wangu mwamuna."