nya-x-nyanja_gen_text_reg/03/17.txt

1 line
416 B
Plaintext

\v 17 Kuli Adamu anakamba kuti, "Cifukwa wa mwera mau ya mkazi wako, wadya kucokela mumtengo, wamene ninaku uza kuti osadyemo,' yotembelereka ni nthaka cifukwa cha iwe; masik yonse uzadya kupitila munchito zobaba. \v 18 Izakulelela minga nazolasa ndipo uzadya vomera mumunda. \v 19 Na cibe capamenso yako uzadya mkate, pakana ubwerere ku dothi, ndaba ndiye kwamene unacoka. Iwe ndiwe dothi, na kudothi uzakabwerela."