nya-x-nyanja_gen_text_reg/14/21.txt

1 line
573 B
Plaintext

\v 21 Mfumu yaku Sondomu inakamba kuti Abramu ati, " Nipase bantu, koma tenga katundu yonse niyako." \v 22 Abramu anakamba kwa mfumu yaku Sodomu ati, " Nanyamula manja ku mwamba kuti yawe, Mulungu waku mwamba mwamba, wolenga ziko yaku mwamba napansi. \v 23 Kuti sinizatengapo kantambo, olo kamagila nsapato, kapena chili chonse cako, kuti usakakambepo, 'Ati ninamulemelesa Abramu.' \v 24 Sinizalenga chili chonse kuchosako chabe vamene anyamata ba ny'ono bany'ono banadiya ndiponso mbuli ya nyamata amene ananipelekeza. Lekani Aneli, Esikolo na mamile dengepo mbali yawo.