nya-x-nyanja_gen_text_reg/24/56.txt

1 line
286 B
Plaintext

\v 56 Koma anabauza kuti, "musanichingilize, chifukwa Yehova ananidalisa munjila yanga. Nitumeni kuti ningayende kuli bwana wanga. \v 57 Banati, "tizamuitana mukazi wamung'ono nakumufunsa." \v 58 Ndipo banamuitana Rebeka nakumufunsa, "uzayenda nauyu mwamuna?"Iye anayankha, "Nizayenda."