nya-x-nyanja_gen_text_reg/24/19.txt

1 line
226 B
Plaintext

\v 19 Pamene anasiliza kumupasa chakumwa, anati, "Nizatapa manzi ya ngamira zako, mpaka zimwe zonse." \v 20 Ndipo anayendesa na kuchosa mu mugomo nakufaka muchomwelamo, nakutamangila kuchisime mukutapa manzi ya ngamira zonse."