nya-x-nyanja_gen_text_reg/24/17.txt

1 line
229 B
Plaintext

\v 17 Ndipo wanchito anatamanga kuti akumane naye nakukamba kuti, napapata nipaseko yang'ono manzi mu mugomo wako. \v 18 Änati, Imwa, bwana wanga,"ndipo anayendesa nakubweza pansi mugomo wake mu manja mwake nakumupasa cha kumwa.