nya-x-nyanja_gen_text_reg/24/12.txt

1 line
559 B
Plaintext

\v 12 Ndipo anati, "Yehova, mulungu wa ba bwana banga ba Abrahamu, nipaseni kupambana ine lelo ndi kukulupilika kwanu muchipangano ndi Bwana wanga Abrahamu. \v 13 Onani, Ine naimilila pa chisime cha manzi, ndipo nana bakazi ba mu muzinda babwela mu kutapa manzi. \v 14 Lekani chichitike motele, nikauza musikana, "napapata bweza pansi mugomo wako kuti nimweko manzi, ndipo azakamba kuti, Imwa, ndipo nizamwesanso na ngamira; wamene uyo ankhale mukazi osankila kapolo wanu Isaki. Pali ichi nizaziba kuti mwalangiza kukulupilika kwa chipangano kwa bwana wanga.