nya-x-nyanja_gen_text_reg/24/10.txt

1 line
359 B
Plaintext

\v 10 Wanchito anatenga kuchokela kwa bwana wake ngamira zili teni ndipo anayambapo. Anatenganso mpaso zosiyana siyana kuchokela kuli ba bwana bake. Ananyamuka na kuyenda ku gawo la Aramu Naharaimu, ku muzinda wa Nahori. \v 11 Anagwadisa ngamira kunja kwa muzinda kuchisime cha manzi. Iyi inali ntawi yakumazulo pamene bakazi banachoka kuyenda mukutapa manzi.