nya-x-nyanja_gen_text_reg/17/19.txt

1 line
496 B
Plaintext

\v 19 Mulungu anati, "Iyayi, koma mukazi wako Sarah azakubalira mwana wamwamuna, ndipo uzaka mupasa zina ya Isaki. Nizakhazikisa chipangano changa ndi iye chifukwa chipangano ndi chamuyayaya na obadwa pa mduyo pake. \v 20 Pali Ishmayeli, nakubvela. Ona, namu dalitsa iye ndipo nizamupanga kuchuluka kwambili. Azakhala tate wabana twove achimu amfumu ndipo azakhala dziko yaikulu. \v 21 Koma chipangano changa niza khazikisa ndi Isaki, wamene Sarah azakubalira iwe pa nthawi ino chaka chitubwera."