nya-x-nyanja_gen_text_reg/17/17.txt

1 line
288 B
Plaintext

\v 17 Abrahamu anagwada nakuika mutu wake pansi, nakuseka ndipo anakamba mumtima wake, " Kodi mwana angabadwe kuli mwamuna alinazaka handiedi? Nizontheka bwanji Sarah, alinazaka naite, kubala mwana mwamuna?" \v 18 Abrahamu anakamba kuli Mulungu kuti, " Ishmaheli azankhalila pamaso panu!"