nya-x-nyanja_gen_text_reg/17/01.txt

1 line
262 B
Plaintext

\c 17 \v 1 Pamene Abramu anali ndi zaka naite naine, Yehohova anaonekela kuli Abramu ndipo anakamba, " Ndine Mulungu wamphavu zonse. Yenda pamanso panga, ndipo nshala ulibe chifukwa. \v 2 Ndipo ndizasimikiza mapangano yanga ndi ine, ndipo muzapaka nakupitilila."