\v 15 Mulungu anakamba kuli Abrahamu kuti, " Mukazi wako Sara, osamuitana futi Sarai. Koma Sarah. \v 16 Nizamudalitsa, ndipo nizakupasa mwana mwamuna muli yeve. Nizamudalitsa, ndipo azankhala mai wamaiko ambiri. Mamfumu abantu azachokela kwa yeve."