Thu Sep 30 2021 19:09:03 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2021-09-30 19:09:04 +02:00
parent 3930351e76
commit 972b4c4700
2 changed files with 2 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 55 \v 56 \v 57 Pamene ziko yonse ya Igupto inali na njala, banthu banaitana kuli kuli Farao kuti abapase vakudya. Ndipo Farao anakamba kuli ba Igupto bonse kuti, Endani kuli Yosefe mukachite vamene eve akamba. Njala inali paliponse paziko yapansi. Yosefe anasegula nkokwe zonse nakugulisa kuli bantu baku Igupto. Njala inakula maningi muziko ya Iguputo. Dziko yonse inali kubwela ku Iguputo kugula tirigu kuli Yosefe, chifukwa njalayo inali itafika poipa kwambiri padziko lonse lapansi.
\v 55 Pamene ziko yonse ya Igupto inali na njala, banthu banaitana kuli kuli Farao kuti abapase vakudya. Ndipo Farao anakamba kuli ba Igupto bonse kuti, Endani kuli Yosefe mukachite vamene eve akamba. \v 56 Njala inali paliponse paziko yapansi. Yosefe anasegula nkokwe zonse nakugulisa kuli bantu baku Igupto. Njala inakula maningi muziko ya Iguputo. \v 57 Dziko yonse inali kubwela ku Iguputo kugula tirigu kuli Yosefe, chifukwa njala ija inali inafika poipa kwambili paziko yonse yapansi.

View File

@ -600,6 +600,7 @@
"41-48",
"41-50",
"41-53",
"41-55",
"42-title",
"42-01",
"42-05",