Sun Oct 10 2021 03:41:55 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2021-10-10 03:41:55 +02:00
parent 4b1dd12671
commit 2ef857e7d8
2 changed files with 1 additions and 1 deletions

1
02/04.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 4 Izi ndizochitika zokhudza kumwamba ndi dziko lapansi pamene zinalengedwa, pa tsiku limene Yehova Mulungu anapanga dziko lapansi ndi zakumwamba. \v 5 Panalibe chitsamba chamtchire padziko lapansi, ngakhale chomera chamthengo sichinamera, pakuti Yehova Mulungu anali asanavumbitsire mvula padziko lapansi, ndipo panalibe munthu wolima nthaka. \v 6 Koma kunkakwera nkhungu yotuluka pansi nathirira dziko lonse lapansi.

View File

@ -55,7 +55,6 @@
"01-30",
"02-title",
"02-01",
"02-07",
"02-09",
"02-11",
"02-13",