Mon Dec 14 2020 15:12:49 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Timothy Muzgatama 2020-12-14 15:12:50 +02:00
parent e846496068
commit 98926ca057
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
Pasiku yamene ija, Farao anapeleka lamulo kuli mabwana bakulu nabo onelela nchito ku bantu. Anakamba, "Kusiyana nakudala, Osabapase bantu uzu paku panga ma buloko. Baleke bayenda kuzitengela mauzu paboka. Koma, mupitilze kubauza kuti bazipanga nambala yama buloko kulingana na yamene banali kupanga kudala. Osavomela chilichonse chachepa apo, chifukwa bali naulesi. Nichifukwa chake bali kuitana na kukamba, Tileke tiyemde anso tikapeleke nsembe kuli Mulungu watu.' Ik
\v 6 Pasiku yamene ija, Farao anapeleka lamulo kuli mabwana bakulu nabo onelela nchito ku bantu. Anakamba, \v 7 "Kusiyana nakudala, Osabapase bantu uzu paku panga ma buloko. Baleke bayenda kuzitengela mauzu paboka. \v 8 Koma, mupitilze kubauza kuti bazipanga nambala yama buloko kulingana na yamene banali kupanga kudala. Osavomela chilichonse chachepa apo, chifukwa bali naulesi. Nichifukwa chake bali kuitana na kukamba, Tileke tiyemde anso tikapeleke nsembe kuli Mulungu watu.' \v 9 Ikilaponi nchito yao amuna kuti bapitiliza kukamba na osaikilako nzelu ku mau yao yabo."