\v 10 Chosalira, limbani mwa Ambuye ndi mu mukulimba kwa mpavu zake. \v 11 Valani chovala cha usilika cha Mulungu, pakuti mukalimbe pa muchenjelelo wa mujelekezi.