\c 6 \v 1 Bana, nvelelani makoro anu mwa Ambuye, chifukwa ichi nichabwino. \v 2 "Lemekeza tate wako ndi mayi” (ili ndiye lamulo loyamba lonkala nachilonjezano), \v 3 ”pakuti zinthu zizikuyendela mushe ndipo unkale ntawi ikulu pa ziko.”