nya-x-nyanja_eph_text_ulb/05/25.txt

1 line
297 B
Plaintext

\v 25 Bamuna, kondani bakazi banu, mwamene Kristu anakondela mupingo ndi kuzipeleka eka mumalo mwake pakuti akaupatule, \v 26 anauwamya ndi ku usuka na manzi na mau, \v 27 pakuti angazipase eka mupingo wa ulemelero, wopanda banga, kapena kwinya, kapena kanthu kotere, koma oyera ndiopanda chilema.