nya-x-nyanja_eph_text_ulb/04/11.txt

1 line
406 B
Plaintext

\v 11 Kristu anapasa bena kunkala ba tumwi, ndipo bena aneneri, ndipo bena balaliki, ndibena ma busa na bapunzisi. \v 12 Anapasa nchinto izi kuti balimbise bantu ba Mulungu kuchita chinto zo sebenza, kumanga tupi ya Kristu. \v 13 Apitiliza kumanga tupi yake panka bonse tikafike kugwilana kwa chikulupiliro na kuziba Mwana wa Mulungu, ndipo kuti tinkale bokula na kufikila kuchipimo chamakulidwe ya Kristu.